Publicidade

1 Timóteo 6

7 Pakuti sitinabweretse kanthu mʼdziko lapansi, ndipo sitingatengenso kanthu pochoka mʼdziko lapansi. 8 Koma ngati tili ndi chakudya ndi zovala, zimenezi zitikwanire.

Veja também

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-29_22-07-56-