21 Ndamupatsa nthawi kuti aleke zachigololo zake koma sakufuna. 22 Tsono ndidzamugwetsa mʼmasautso ndipo amene amachita naye zadama zakezo ndidzawasautsa kwambiri akapanda kulapa ndi kuleka njira za mkaziyo.
Publicidade