5 Amene anakhala pa mpando waufumuyo anati, "Ndikulenga zinthu zonse zikhale zatsopano!" Ndipo anati, "Lemba izi, pakuti mawu awa ndi okhulupirika ndi woona."