Pular para o conteúdo
Publicidade

MACHITIDWE A ATUMWI 18

9 Usiku wina Ambuye anaonekera kwa Paulo mʼmasomphenya namuwuza kuti, "Usaope, pitiriza kuyankhula, usakhale chete. 10 Pakuti Ine ndili nawe, palibe aliyense amene adzakukhudza ndi kukuchitira choyipa, chifukwa mu mzinda muno ndili ndi anthu ambiri."

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também