18Anthu oyenda pa ngamira amapatukirako kufuna madzi;iwo amangoyendayenda nʼkufera mʼchipululu.
Resultados da busca por "fé"
27 resultados encontrados
- Capítulo 6
Jó 6
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 18 de 30 - Capítulo 7
1 Reis 7
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 5 de 515Zitseko zonse ndi mazenera omwe, maferemu ake anali ofanana mbali zonse. Mulitali mwake ndi mulifupi mwake, ndipo zenera linkapenyana ndi zenera linzake pa mizere itatu.
- Capítulo 37
Êxodo 37
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 12 de 2912Iwo anapanga feremu yozungulira tebulo, mulifupi mwake ngati chikhatho cha dzanja, ndipo anayika mkombero wagolide kuzungulira feremuyo.
- Capítulo 26
Atos 26
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 24 de 3224Paulo akudziteteza, Festo anakweza mawu nati, "Wazungulira mutu Paulo! Kuphunzira kwako kwakuchititsa misala."
- Capítulo 26
Êxodo 26
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 1 de 371"Panga chihema pogwiritsa ntchito nsalu khumi zofewa, zosalala ndi zolukidwa bwino, zobiriwira, zapepo ndi zofiira. Ndipo anthu aluso apete pa nsaluzo Akerubi.
- Capítulo 23
Atos 23
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 9 de 359Panali phokoso lalikulu, ndipo aphunzitsi ena amalamulo amene anali a gulu la Afarisi anayimirira natsutsa kwambiri. Iwo anati, "Ife sitikupeza cholakwa ndi munthu uyu, chifukwa mwina ndi mzimu kapena mngelo amene wayankhula naye."
- Capítulo 36
Êxodo 36
Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa ChaleroMostrando versículo 8 de 388Anthu onse aluso pakati pa anthu ogwira ntchitoyo anapanga chihema pogwiritsa ntchito nsalu khumi zofewa, zosalala ndi zolukidwa bwino, zobiriwira, zapepo ndi zofiira. Ndipo anthu aluso anapeta pa nsaluzo Akerubi.