Pular para o conteúdo
Publicidade

Resultados da busca por "fé"

27 resultados encontrados

  1. Romanos 16

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 16
    Mostrando versículo 1 de 27

    1Ine ndikupereka kwa inu mlongo wathu Febe, mtumiki wa mpingo wa ku Kenkreya.

  2. Êxodo 16

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 16
    Mostrando versículo 3 de 36

    3kuti, "Kukanakhala bwino Yehova akanatiphera mʼdziko la Igupto! Kumeneko timadya nyama ndi buledi mpaka kukhuta, koma inu mwabwera nafe ku chipululu kudzapha mpingo wonsewu ndi njala!"

  3. 2 Timóteo 4

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 4
    Mostrando versículo 12 de 22

    12Ndatumiza Tukiko ku Efeso.

  4. Josué 12

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 12
    Mostrando versículo 17 de 24

    17mfumu ya Tapuwa imodzimfumu ya Heferi imodzi

  5. Salmos 89

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 89
    Mostrando versículos 14–45 de 52

    14Chilungamo ndi chiweruzo cholungama ndiye maziko a mpando wanu waufumu;chikondi ndi kukhulupirika zimayenda patsogolo panu.

    37udzakhazikika kwamuyaya monga mwezi,mboni yokhulupirika mʼmitambo.Sela

    45Mwachepetsa masiku a unyamata wake;mwamuphimba ndi chofunda chochititsa manyazi.Sela

  6. Ezequiel 45

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 45
    Mostrando versículos 10–21 de 25

    10Miyeso yanu yoyezera zinthu monga efa ndi bati zizikhala zokhulupirika.

    11Efa ndi bati ikhale miyeso yolingana kukula kwake. Muyeso wa homeri ukhale wokwanira mabati khumi, ukhalenso wokwanira maefa khumi. Ndiye kuti kukula kwa miyeso iwiriyo kuzidzatsata kukula kwa homeriyo.

    21" ‘Pa tsiku la 14 la mwezi woyamba muzichita chikondwerero cha Paska, chikondwerero chake cha masiku asanu ndi awiri. Pa masiku amenewo muzidzadya buledi wopanda yisiti.

  7. Oséias 5

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 5
    Mostrando versículo 3 de 15

    3Ndimadziwa zonse za Efereimu;Aisraeli ndi osabisika kwa Ine.Efereimu wayamba tsopano kuchita zachiwerewere;Israeli wadziyipitsa.

  8. Números 26

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 26
    Mostrando versículo 11 de 65

    11Koma ana a Kora sanafe nawo.

  9. 1 Coríntios 16

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 16
    Mostrando versículo 8 de 24

    8Koma ndikhala ndili ku Efeso mpaka nthawi ya Pentekosite,

  10. Números 13

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 13
    Mostrando versículo 7 de 33

    7kuchokera ku fuko la Isakara, Igala mwana wa Yosefe;

  11. Marcos 4

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 4
    Mostrando versículo 3 de 41

    3"Tamverani! Mlimi anapita kukafesa mbewu zake.

  12. Salmos 20

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 20
    Mostrando versículo 5 de 9

    5Ife tidzafuwula ndi chimwemwe pamene iwe wapambanandipo tidzanyamula mbendera zathu mʼdzina la Mulungu wathu,Yehova ayankhe zopempha zako zonse.

  13. Oséias 4

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 4
    Mostrando versículo 17 de 19

    17Efereimu waphathana ndi mafano;mulekeni!

  14. Efésios 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículo 1 de 23

    1Paulo, mtumwi wa Khristu Yesu mwachifuniro cha Mulungu.Kulembera oyera mtima a ku Efeso, okhulupirika mwa Khristu Yesu:

  15. João 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículo 14 de 51

    14Mawu anasandulika thupi ndipo anakhala pakati pathu. Ife tinaona ulemerero wake, ulemerero wa Iye amene ndi Mwana mmodzi yekhayo wa Atate, wodzaza ndi chisomo ndi choonadi.

  16. 1 Crônicas 7

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 7
    Mostrando versículo 15 de 40

    15Makiri anatenga mkazi wa banja la Ahupi ndi Asupi. Mlongo wake anali Maaka.Mwana wake wina anali Zelofehadi, amene anabereka ana aakazi okhaokha.

  17. Neemias 12

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 12
    Mostrando versículo 14 de 47

    14wa fuko la Maluki anali Yonatani;wa fuko la Sebaniya anali Yosefe;

  18. Atos 24

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 24
    Mostrando versículo 2 de 27

    2Atamuyitana Paulo, ndipo Tertuliyo anafotokozera Felike nkhani yonse ya Paulo. Iye anati, "Wolemekezeka, ife takhala pamtendere nthawi yayitali chifukwa cha inu, ndipo utsogoleri wanu wanzeru wabweretsa kusintha mʼdziko lino.

  19. Atos 25

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 25
    Mostrando versículo 1 de 27

    1Patapita masiku atatu Festo atafika mʼdera lake, anachoka ku Kaisareya ndi kupita ku Yerusalemu.

  20. Êxodo 25

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 25
    Mostrando versículo 4 de 40

    4Nsalu zobiriwira, zapepo, zofiira, nsalu zofewa, ubweya wambuzi;

Léxico (correspondência exata) Semântico (correspondência relacionada) Versículos omitidos Contexto do capítulo