Pular para o conteúdo
Publicidade

Resultados da busca por "salvação"

57 resultados encontrados

  1. Isaías 38

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 38
    Mostrando versículos 14–20 de 22

    14Ndinkalira ngati namzeze kapena chumba,ndinkabuwula ngati nkhunda yodandaula.Maso anga anatopa nʼkuyangʼana mlengalenga.Inu Ambuye, ine ndili mʼmavuto bwerani mudzandithandize!"

    16Ambuye, masiku anga ali mʼmanja mwanu.Mzimu wanga upeza moyo mwa Inu.Munandichiritsa ndikundikhalitsa ndi moyo.

    20Yehova watipulumutsa.Tiyeni tiyimbe ndi zoyimbira za zingwemasiku onse a moyo wathumʼNyumba ya Yehova.

  2. 2 Reis 18

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 18
    Mostrando versículos 32–34 de 37

    32mpaka nditabwera kudzakutengani kupita ku dziko lofanana ndi lanuli, dziko la tirigu ndi vinyo watsopano, dziko la chakudya ndi minda ya mipesa, dziko la mitengo ya olivi ndi uchi. Sankhani moyo osati imfa!"Musamvere zonena Hezekiya, pakuti iye akukusocheretsani ponena kuti, ‘Yehova adzatipulumutsa.’

    33Kodi mulungu wa anthu a mtundu wina uliwonse wapulumutsapo dziko lake mʼdzanja la mfumu ya ku Asiriya?

    34Kodi ili kuti milungu ya Hamati ndi Aripadi? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu, Hena ndi Ivani? Kodi inapulumutsa Samariya mʼdzanja langa?

  3. Jeremias 20

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 20
    Mostrando versículos 13–16 de 18

    13Imbirani Yehova!Mutamandeni Yehova!Iye amapulumutsa wosaukamʼmanja mwa anthu oyipa.

    14Litembereredwe tsiku limene ndinabadwa!Tsiku limene amayi anga anandibereka lisatamandidwe!

    16Munthu ameneyo akhale ngati mizinda imeneYehova anayiwononga mopanda chisoni.Amve mfuwu mmawa,phokoso la nkhondo masana.

  4. Jó 14

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 14
    Mostrando versículos 3–14 de 22

    3Kodi munthu wotereyo nʼkumuyangʼanitsitsa?Kodi mungamubweretse pamaso panu kuti mumuzenge mlandu?

    4Ndani angatulutse chabwino mʼchoyipa?Palibe ndi mmodzi yemwe!

    14Munthu akafa, kodi adzakhalanso ndi moyo?Masiku anga onse a moyo wovutikawundidzadikira mpaka itafika nthawi yomasulidwa.

  5. 2 Tessalonicenses 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 1–7 de 12

    1Paulo, Silivano ndi Timoteyo.Kulembera mpingo wa ku Tesalonika, umene uli mwa Mulungu Atate athu ndi Ambuye Yesu Khristu.

    6Mulungu ndi wolungama ndipo adzalanga amene amakusautsaniwo

    7ndikukupatsani mpumulo amene mukusautsidwa, pamodzi ndi ifenso. Izi zidzachitika Ambuye Yesu akadzaoneka mʼmalawi amoto kuchokera kumwamba pamodzi ndi angelo ake amphamvu.

  6. Êxodo 26

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 26
    Mostrando versículos 12–34 de 37

    12Theka lotsalira la nsaluyo lidzalendewera kumbuyo kwa chihemacho.

    13Nsalu yotsalira ya masentimita 46 mulitali mwake mʼmbali zonse ziwiri idzalendewere kuphimba mbali ziwirizo.

    34Uyike chivundikiro pa bokosi laumboni ku malo wopatulika kwambiri.

  7. Mateus 18

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 18
    Mostrando versículos 4–11 de 35

    4Chifukwa chake, aliyense amene adzichepetsa yekha ngati kamwana aka, ameneyo ndiye wamkulu koposa onse mu ufumu wakumwamba.

    8Ngati dzanja lako kapena phazi lako likuchimwitsa, lidule ndi kulitaya. Ndi bwino kwa iwe kulowa mʼmoyo wosatha wolumala kusiyana ndi kukhala ndi manja awiri kapena mapazi awiri ndi kukaponyedwa ku moto wosatha.

    11(Mwana wa Munthu anabwera kudzapulumutsa chimene chinatayika).

  8. Provérbios 14

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 14
    Mostrando versículos 12–27 de 35

    12Pali njira ina yooneka ngati yabwino kwa munthu,koma kumatsiriziro kwake ndi ku imfa.

    25Mboni yokhulupirika imapulumutsa miyoyo,koma mboni yabodza imaphetsa.

    27Kuopa Yehova ndiye kasupe wamoyo,kumathandiza munthu kuti apewe msampha wa imfa.

  9. Números 33

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 33
    Mostrando versículos 15–22 de 56

    15Atachoka ku Refidimu anakamanga ku chipululu cha Sinai

    21Atachoka ku Libina anakamanga ku Risa.

    22Atachoka ku Risa anakamanga ku Kehelata.

  10. Tiago 4

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 4
    Mostrando versículos 2–8 de 17

    2Mumalakalaka zinthu koma simuzipeza, choncho mumapha. Mumasirira zinthu koma simutha kuzipeza zimene mukufuna, choncho mumakangana ndi kumenyana. Mulibe zinthuzo chifukwa simupempha kwa Mulungu.

    7Dziperekeni nokha kwa Mulungu. Mukaneni Mdierekezi ndipo adzakuthawani.

    8Sendezani kufupi ndi Mulungu ndipo Iye adzasendeza kwa inu. Sambani mʼmanja mwanu, inu anthu ochimwa. Yeretsani mitima yanu, inu anthu okayikira.

  11. Neemias 10

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 10
    Mostrando versículos 3–25 de 39

    3Pasuri, Amariya, Malikiya,

    12Zakuri, Serebiya, Sebaniya,

    25Rehumu, Hasabiya, Maaseya,

  12. João 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 2–16 de 51

    2Mawuwa anali ndi Mulungu pachiyambi.

    9Kuwunika koona kumene kuwunikira munthu aliyense kunabwera ku dziko lapansi.

    16Kuchokera mʼkuchuluka kwa chisomo chake ife tonse talandira madalitso pamwamba pa madalitso.

  13. Salmos 32

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 32
    Mostrando versículos 1–7 de 11

    1Ngodala munthuamene zolakwa zake zakhululukidwa;amene machimo ake aphimbidwa.

    5Kotero ine ndinavomereza tchimo langa kwa Inu,sindinabise mphulupulu zanga.Ndinati, "Ine ndidzawululazolakwa zanga kwa Yehova,ndipo Inu munandikhululukiramlandu wa machimo anga."Sela

    7Inu ndi malo anga obisala;muzinditeteza ku mavuto ndipo muzindizingandi nyimbo zachipulumutso.Sela

  14. Êxodo 30

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 30
    Mostrando versículos 1–31 de 38

    1Upange guwa lamatabwa amtengo wa mkesha lofukizirapo lubani.

    26Tsono uwagwiritse ntchito podzoza tenti ya msonkhano, Bokosi la Chipangano,

    31Tsono awuze a Israeli kuti, mafuta wodzozera awa adzakhala wopatulika mpaka muyaya.

  15. Atos 11

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 11
    Mostrando versículos 9–25 de 30

    9"Mawu ochokera kumwamba ananenanso kachiwiri kuti, ‘Chimene Mulungu wachiyeretsa usanene kuti ndi chodetsedwa.’

    14Iye adzakuwuza uthenga umene udzapulumutsa iwe ndi a pa banja ako.’

    25Kenaka Barnaba anapita ku Tarisisi kukafuna Saulo,

  16. Levítico 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 4–13 de 17

    4Munthuyo asanjike dzanja lake pa mutu pa nsembe yopserezayo, ndipo idzalandiridwa kuti ikhale yopepesera machimo ake.

    6Munthuyo asende nsembe yopserezayo ndi kuyidula nthulinthuli.

    13Munthuyo atsuke zamʼkati mwa nyamayo pamodzi ndi miyendo yake yomwe, ndipo wansembe abwere nazo zonse ndi kuzitentha pa guwa. Iyi ndi nsembe yopsereza, chopereka chotentha pa moto, fungo lokomera Yehova.

  17. 1 Crônicas 14

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 14
    Mostrando versículos 5–7 de 17

    5Ibihari, Elisua, Elipeleti,

    6Noga, Nefegi, Yafiya,

    7Elisama, Beeliada ndi Elifeleti.

  18. Deuteronômio 23

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 23
    Mostrando versículos 1–12 de 25

    1Mwamuna aliyense wofulidwa kapena woduka chiwalo chachimuna asalowe nawo mu msonkhano wa Yehova.

    11Koma dzuwa likapendeka ayenera kusamba ndipo polowa dzuwa akhoza kubwerera ku msasa.

    12Mukonze malo kunja kwa msasa kumene mukhoza kukadzithandizirako.

  19. Efésios 6

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 6
    Mostrando versículos 14–17 de 24

    14Tsono imani mwamphamvu, mutamangira choonadi ngati lamba mʼchiwuno mwanu, mutavala chilungamo ngati chitsulo chotchinjiriza pa chifuwa.

    15Valani Uthenga Wabwino wamtendere ku mapazi anu ngati nsapato.

    17Valani chipewa cha chipulumutso ndi kutenga lupanga la mzimu, limene ndi Mawu a Mulungu.

  20. Tito 2

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 2
    Mostrando versículos 9–13 de 15

    9Phunzitsa akapolo kuti azigonjera ambuye awo mu zinthu zonse ndi kuwakondweretsa. Asamatsutsane nawo

    11Pakuti chisomo cha Mulungu chimene chimapulumutsa chaonekera kwa anthu onse.

    13pamene tikudikira chiyembekezo chodala; kuonekera kwa ulemerero wa Mulungu wathu wamkulu ndi Mpulumutsi, Yesu Khristu,

Léxico (correspondência exata) Semântico (correspondência relacionada) Versículos omitidos Contexto do capítulo