Pular para o conteúdo
Publicidade

Resultados da busca por "salvação"

57 resultados encontrados

  1. Salmos 3

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 3
    Mostrando versículos 2–8 de 8

    2Ambiri akunena za ine kuti,"Mulungu sadzamupulumutsa."Sela

    7Dzukani, Inu Yehova!Pulumutseni, Inu Mulungu wanga.Akantheni adani anga onse pa msagwada;gululani mano a anthu oyipa.

    8Chipulumutso chimachokera kwa Yehova.Madalitso akhale pa anthu anu.Sela

  2. Jó 33

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 33
    Mostrando versículos 18–30 de 33

    18kumulanditsa munthu ku manda,kuti moyo wake usawonongeke ndi lupanga.

    24kudzamukomera mtima ndi kunena kuti,‘Mupulumutseni kuti asapite ku manda;ine ndapeza cholowa mʼmalo mwa moyo wake,’

    30kupulumutsa moyo wa munthuyo ku manda,kuti athe kuonanso kuwala kwa moyo.

  3. Salmos 89

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 89
    Mostrando versículos 37–48 de 52

    37udzakhazikika kwamuyaya monga mwezi,mboni yokhulupirika mʼmitambo.Sela

    45Mwachepetsa masiku a unyamata wake;mwamuphimba ndi chofunda chochititsa manyazi.Sela

    48Kodi ndi munthu uti angakhale ndi moyo ndi kusaona imfa?Kapena kudzipulumutsa yekha ku mphamvu ya manda?Sela

  4. Lamentações 3

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 3
    Mostrando versículos 26–38 de 66

    26nʼkwabwino kudikira chipulumutso chaYehova modekha.

    35kukaniza munthu ufulu wakepamaso pa Wammwambamwamba,

    38Kodi zovuta ndi zabwino sizitulukamʼkamwa mwa Wammwambamwamba?

  5. Romanos 7

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 7
    Mostrando versículos 12–24 de 25

    12Choncho lamulo ndi loyera, lolungama ndi labwino.

    22Mtima wanga umakondwera ndi lamulo la Mulungu.

    24Kalanga ine! Adzandipulumutsa ndani ku thupi la imfali?

  6. Provérbios 23

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 23
    Mostrando versículos 11–14 de 35

    11paja Mpulumutsi wawo ndi wamphamvu;iye adzawateteza pa milandu yawo kutsutsana nawe.

    13Usaleke kumulangiza mwana;ngati umulanga ndi chikwapu sadzafa.

    14Ukamukwapula ndi tsatsaudzapulumutsa moyo wake.

  7. Números 6

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 6
    Mostrando versículos 6–24 de 27

    6Pa nthawi yonse imene munthuyo wadzipatula yekha kwa Yehova asayandikire mtembo.

    8Munthuyo ndi wopatulika masiku onse odzipereka kwake kwa Yehova.

    24" ‘Yehova akudalitsendi kukusunga;

  8. Habacuque 3

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 3
    Mostrando versículos 5–18 de 19

    5Patsogolo pake pankagwa mliri;nthenda yoopsa inkagwa kumbuyo kwake.

    13Munapita kukalanditsa anthu anu,kukapulumutsa wodzozedwa wanu.Munakantha mtsogoleri wa dziko la anthu oyipa,munawononga anthu ake onse.Sela

    18komabe ine ndidzakondwera mwa Yehova,ndidzasangalala mwa Mulungu Mpulumutsi wanga.

  9. Lucas 20

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 20
    Mostrando versículos 30–43 de 47

    30Wachiwiri

    32Pa mapeto pake mkaziyo anafanso.

    43mpaka Ine nditasandutsa adani anuchopondapo mapazi anu?’

  10. 1 Pedro 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 4–9 de 25

    4kuti tidzalandire chuma chomwe sichingawonongeke, kuyipitsidwa kapena kufota. Chuma chimenechi akukusungirani kumwamba.

    5Mwachikhulupiriro, mukusungidwa ndi mphamvu ya Mulungu mpaka chipulumutso chitafika chimene chinakonzedwa kuti adzachionetse nthawi yotsiriza.

    9Motero mukulandira mphotho ya chikhulupiriro chanu, ndiyo chipulumutso cha moyo wanu.

  11. Lucas 21

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 21
    Mostrando versículos 13–22 de 38

    13Umenewu udzakhala mwayi wanu ochitira umboni.

    19Mukadzalimbikira ndiye mudzapeze moyo.

    22Pakuti iyi ndi nthawi yachilango pokwaniritsa zonse zimene zinalembedwa.

  12. Esdras 10

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 10
    Mostrando versículos 37–42 de 44

    37Mataniya, Matenayi ndi Yasu.

    40Makinadebayi, Sasai, Sarai,

    42Salumu, Amariya ndi Yosefe.

  13. Gênesis 49

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 49
    Mostrando versículos 3–31 de 33

    3"Rubeni, ndiwe woyamba kubadwa;mphamvu yanga ndiponso chizindikiro choyamba cha mphamvu zanga,wopambana pa ulemerero ndi mphamvu.

    18"Ndikuyembekeza chipulumutso chanu Yehova.

    31Kumeneko kunayikidwa Abrahamu ndi mkazi wake Sara, Isake ndi mkazi wake Rebeka ndipo ndinayikakonso Leya.

  14. Efésios 4

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 4
    Mostrando versículos 5–26 de 32

    5Pali Ambuye mmodzi, chikhulupiriro chimodzi, ubatizo umodzi;

    9Kodi mawu akuti, "Iye anakwera" akutanthauza chiyani, ngati Iyeyo sanatsikire kunsi kwa dziko lapansi?

    26Kwiyani koma musachimwe. Dzuwa lisalowe mukanali chikwiyire.

  15. Mateus 24

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 24
    Mostrando versículos 8–28 de 51

    8Zonsezi ndi chiyambi chabe cha zowawa.

    13koma wopirira kufikira chimaliziro adzapulumuka.

    28Kulikonse kuli chinthu cha kufa, makwangwala adzasonkhanako.

  16. Isaías 12

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 12
    Mostrando versículos 2–5 de 6

    2Zoonadi, Mulungu ndiye Mpulumutsi wanga;ndidzamudalira ndipo sindidzachita mantha.Yehova ndiye mphamvu yanga ndi nyimbo yanga;Iye wakhala chipulumutso changa."

    3Mudzakondwera popeza Yehovaali ngati chitsime cha chipulumutso chanu.

    5Imbirani Yehova, pakuti wachita ntchito zazikulu;zimenezi zidziwike pa dziko lonse lapansi.

  17. 1 Crônicas 6

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 6
    Mostrando versículos 12–53 de 81

    12Ahitubi anabereka Zadoki,Zadoki anabereka Salumu,

    24Tahati, Urieli,Uziya ndi Sauli.

    53Zadokindi Ahimaazi.

  18. 1 Coríntios 15

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 15
    Mostrando versículos 20–46 de 58

    20Koma nʼzoonadi kuti Khristu anaukitsidwa kwa kufa, chipatso choyamba cha onse ogona tulo.

    26Mdani wotsiriza kuwonongedwa ndi imfa.

    46Zauzimu sizinabwere koyambirira, koma zachilengedwe, pambuyo pake zauzimu.

  19. Levítico 16

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 16
    Mostrando versículos 25–31 de 34

    25Mafuta a nyama yopepesera machimo awatenthe pa guwa lansembe.

    28Munthu amene azitenthe achape zovala zake ndi kusamba. Pambuyo pake alowe mu msasa.

    31Limeneli ndi tsiku lanu la Sabata lopumula, ndipo muzigonja pamaso pa Yehova. Limeneli ndi lamulo lanu la muyaya.

  20. Cânticos 2

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 2
    Mostrando versículos 1–15 de 17

    1Ine ndine duwa la ku Saroni,duwa lokongola la ku zigwa.Mwamuna

    2Monga duwa lokongola pakati pa mingandi momwe alili wokondedwa wanga pakati pa atsikana.Mkazi

    15Mutigwirire nkhandwe,nkhandwe zingʼonozingʼonozimene zikuwononga minda ya mpesa,minda yathu ya mpesa imene yayamba maluwa.Mkazi

Léxico (correspondência exata) Semântico (correspondência relacionada) Versículos omitidos Contexto do capítulo