1 Choncho, monga ana okondedwa, tsatirani chitsanzo cha Mulungu. 2 Muzikondana monga Khristu anakonda ife nadzipereka yekha chifukwa cha ife monga chopereka cha fungo lokoma ndi nsembe kwa Mulungu.