Publicidade

Ezequiel 37

4 Pamenepo anandiwuza kuti, "Lengeza kwa mafupa amenewa ndi kuwawuza kuti amve mawu a Ine Yehova! 5 Uwawuze kuti zimene Ine Ambuye Yehova ndikunena kwa mafupa ndi izi: Ndidzawuzira mpweya mwa inu, ndipo mudzakhalanso ndi moyo.

Veja também

Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-07-05_19-25-13-