Pular para o conteúdo
Publicidade

Agalatiya 6:1-5

TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

Kuchita Zabwino kwa Onse

1 Abale, ngati munthu agwa mʼtchimo lililonse, inu amene Mzimu amakutsogolerani, mumuthandize munthuyo ndi mtima wofatsa kuti akonzekenso. Koma mukhale maso kuti inu nomwe mungayesedwe. 2 Thandizanani kusenza zolemetsa zanu, ndipo mʼnjira imeneyi mudzakwanitsa lamulo la Khristu. 3 Ngati wina adziyesa kanthu pamene iyeyo sali kanthu konse, akudzinamiza yekha. 4 Munthu aliyense aziyesa yekha ntchito zake mmene zilili. Ngati zili bwino, adzatha kunyadira chifukwa cha ntchito zake zokhazo, iyeyo asadzifanizire ndi munthu wina wake, 5 pakuti aliyense ayenera kusenza katundu wake.

Em outras traduções

  1. NTNYBL2025 Nyanja

    1 Abale wanga ngati mkamwona mundhu fulani walakwila, basi anyiimwe mchogozedwa ni mzimu wa Mnungu muonyeni mundhu mmeneyo wasiye vichito vake, nambho mchite chimwecho kwa upole, mku ni mjhipenyelela dala mwachinawene simdalowa mmayeso. 2 Mthangatilane anyiimwe kwa anyiimwe kwakuchita chimwecho simkwanilichwe thauko la Kilisito. 3 Mundhu waliyonjhe wakajhiona kuti iye ni wamate, nikumbe osati wamate wajhinyenga mwene. 4 Nambho kila mundhu wajhipenyecheche mwene. Ngati ivo wavichita ni vabwino pamenepo siwakhale ni ndande ya kujhidama mkati mwake ni asati mkati mwa mnjake. 5 Pakuti kila mundhu siwalangidwe kuchokana ni vichito vake.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.