Publicidade

Hebreus 13

5 Mtima wanu usakonde ndalama koma mukhutitsidwe ndi zimene muli nazo, chifukwa Mulungu anati,

"Sadzakusiyani,

kapena kukutayani konse."

6 Kotero ife tikunena molimba mtima kuti,

"Ambuye ndiye mthandizi wanga;

sindidzachita mantha. Munthu angandichitenji ine?"

Veja também

Publicidade
Hebreus
Ver todos os capítulos de Hebreus
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-22_10-02-25-