21 nati,
"Ndinatuluka maliseche mʼmimba mwa amayi anga,
namonso mʼmanda ndidzalowa wamaliseche.
Yehova ndiye anapereka ndipo Yehova watenga;
litamandike dzina la Yehova."
22 Mu zonsezi, Yobu sanachimwe kapena kunena kuti, "Mulungu walakwa."