Fanizo la Nkhosa Yotayika
1 Tsopano amisonkho ndi "ochimwa" ankasonkhana kudzamvera mawu ake. 2 Koma Afarisi ndi aphunzitsi amalamulo amangʼungʼudza nati, "Munthu uyu amalandira ochimwa ndi kudya nawo."