22 Kodi ndi bwino kwa ife kumapereka msonkho kwa Kaisara kapena kusapereka?"
23 Iye anaona chinyengo chawo ndipo anawawuza kuti, 24 "Onetseni ndalama. Chithunzi ndi malembawa ndi zayani?"
25 Iwo anayankha kuti, "Za Kaisara."
Iye anawawuza kuti, "Ndiye perekani kwa Kaisara zake za Kaisara ndi kwa Mulungu zimene ndi za Mulungu."