Pular para o conteúdo
Publicidade

Luka 20:22-25

NTNYBL2025 Nyanja

22 Tikambileni, bwanji, thauko la Musa litilola kulipila malipilo kwa mfumu wa mkulu wa Aloma?"

23 Nambho Yesu wadajhiwa msambha wawo, wadaakambila, 24 "Nilangizeni gelenjha. Bwanji, chitunjhi ichi ni malembo yali pamwamba ni yayani?"

25 Anyiiwo adamuyangha, "Ni ya Kaisali, mfumu wamkulu wa Aloma." Ndiipo Yesu wadaakambila, "Mpacheni Kaisali mfumu wamkulu wa Aloma icho chili cha mfumu wa Aloma, ni mpacheni Mnungu icho chili cha Mnungu."

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    22 Kodi ndi bwino kwa ife kumapereka msonkho kwa Kaisara kapena kusapereka?"

    23 Iye anaona chinyengo chawo ndipo anawawuza kuti, 24 "Onetseni ndalama. Chithunzi ndi malembawa ndi zayani?"

    25 Iwo anayankha kuti, "Za Kaisara."

    Iye anawawuza kuti, "Ndiye perekani kwa Kaisara zake za Kaisara ndi kwa Mulungu zimene ndi za Mulungu."

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.