Pular para o conteúdo
Publicidade

Mateus 12

10 Ndipo mʼmenemo munali munthu wolumala dzanja. Pofuna chifukwa chokamunenezera, iwo anamufunsa Yesu kuti, "Kodi nʼkololedwa kuchiritsa munthu tsiku la Sabata?"

11 Iye anawawuza kuti, "Ngati wina wa inu ali ndi nkhosa nigwera mʼdzenje tsiku la Sabata, kodi simudzayigwira ndi kuyitulutsa kunja? 12 Nanga munthu sali oposa nkhosa kwambiri! Chifukwa chake nʼkololedwa kuchita zabwino pa Sabata."

13 Pamenepo Yesu anati kwa munthuyo, "Wongola dzanja lako." Iye analiwongola ndipo linakhala monga linalili kale.

Veja também