Pular para o conteúdo
Publicidade

MATEYU 26

26 Pamene ankadya, Yesu anatenga buledi, nayamika ndipo anamunyema nagawira ophunzira ake nanena kuti, "Tengani, idyani; ili ndi thupi langa."

27 Kenaka anatenga chikho, nayamika nachipereka kwa iwo nati, "Imwani nonsenu. 28 Awa ndi magazi anga a pangano amene akhetsedwa chifukwa cha ambiri kuti akhululukidwe machimo.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também