32 Pamene iwo ankatuluka kunja, anthu anabwera kwa Iye ndi munthu wogwidwa ndi mzimu wosayankhula. 33 Ndipo atatulutsa mzimuwo, munthuyo anayankhula. Gulu la anthuwo linadabwa ndipo linati, "Zinthu zotere sizinaonekepo mu Israeli."
Publicidade

+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.