Pular para o conteúdo
Publicidade

NEHEMIYA 2

17 Ndinawawuza kuti, "Inu mukuona mavuto amene tili nawo. Mukuona kuti mzinda wa Yerusalemu wasanduka bwinja ndipo zipata zake zatenthedwa ndi moto. Tsono tiyeni timangenso makoma a Yerusalemu ndipo sitidzachitanso manyazi."

Veja também