Pular para o conteúdo
Publicidade

AROMA 9

20 Koma ndiwe yani, munthu wamba, woti nʼkutsutsana ndi Mulungu? "Kodi chimene chinawumbidwa nʼkufunsa amene anachiwumba kuti, Kodi unandiwumbiranji motere?’ " 21 Kodi wowumba alibe ufulu wowumba kuchokera ku dothi lomwelo mbiya yamtengowapatali ndi ina yamtengo wotsika?

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também