Pular para o conteúdo
Publicidade

TITO 3

4 Koma kukoma mtima ndi chikondi cha Mulungu Mpulumutsi wathu chitaonekera, 5 Iye anatipulumutsa, osati chifukwa cha ntchito zathu zolungama zimene tinachita koma chifukwa cha chifundo chake. Anatipulumutsa potisambitsa, kutibadwitsa kwatsopano ndi kutikonzanso mwa Mzimu Woyera 6 amene anatipatsa mowolowamanja kudzera mwa Yesu Khristu Mpulumutsi wathu,

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também

Tito
Ver todos os capítulos de Tito