Pular para o conteúdo
Publicidade

Liberdade

Por Bíblia Online

Cristo nos libertou para a liberdade. A Bíblia proclama a libertação do pecado, da condenação e de toda forma de escravidão espiritual. Na verdade de Cristo, somos verdadeiramente livres.

Liberdade em Cristo

Para a liberdade Cristo nos libertou. Se o Filho vos libertar, verdadeiramente sereis livres. Não volteis ao jugo da escravidão.

Muusunge ufulu wanu

Kilisito wadatipacha ife ufulu, iye wadafuna tikhale afulu, chipano imani nganga simdavomela kukhalanjho pajhi pa ukapolo.

Muusunge ufulu wanu

Kilisito wadatipacha ife ufulu, iye wadafuna tikhale afulu, chipano imani nganga simdavomela kukhalanjho pajhi pa ukapolo.

Mwana wakakuchitani mlekeleledwe simulekeleledwe zenezene.

Mwana wakakuchitani mlekeleledwe simulekeleledwe zenezene.

Uzene siukulekeleleni

Ndiipo, Yesu wadaakambila Ayahudi yawo adamkhulupilila, "Mkayagwila mayaluzo yanga simukhale oyaluzidwa wanga azene. Simuujhiwe uzene, ni uzene siukulekeleleni."

Uzene siukulekeleleni

Ndiipo, Yesu wadaakambila Ayahudi yawo adamkhulupilila, "Mkayagwila mayaluzo yanga simukhale oyaluzidwa wanga azene. Simuujhiwe uzene, ni uzene siukulekeleleni."

Livres da condenação

Não há condenação para os que estão em Cristo Jesus. A lei do Espírito nos libertou da lei do pecado e da morte.

Kukhala kwa mbhavu za Mzimu wa Mnungu

Chipano palibe lamulo la chilango kwa anyiwajha yao muukhalo wao alunjana ni Kilisito. Pakuti thauko la Mzimu ilo lipeleka umoyo kwa kulanjana ni kilisito Yesu, yanilekelela kuchokela mthauko la machimo ilo lipeleka nyifa.

Kukhala kwa mbhavu za Mzimu wa Mnungu

Chipano palibe lamulo la chilango kwa anyiwajha yao muukhalo wao alunjana ni Kilisito. Pakuti thauko la Mzimu ilo lipeleka umoyo kwa kulanjana ni kilisito Yesu, yanilekelela kuchokela mthauko la machimo ilo lipeleka nyifa. Mnungu wadachita chindhu chijha thauko silidakhoze kuchita, ndande ya kuchepekela kwa Mundhu. Mnungu wadamtuma Mwana wake uku wali ni thupi ngati umo tili ife, dala wayachoche machimo kwa thupi lake, ni kwa thupi limwelo wayachoche machimo. Mnungu wadachita chimwecho kuti tikhoze kuchita yajha yafunika ni thauko, kwa kumkhulupilila mzimu wa Mnungu pambuyo pa kuyavela makhumbilo ya matupi yathu.

Pakuti voumbidwa vonjhe vidaikidwa mosajhikozela, osati kwa kufuna kwao, nambho vidachitidwa chimwecho ngati umo wadafunila Mnungu. Ata chimwecho chilipo chikulupililo, pakuti voumbidwa vimenevo navo siviomboledwe kuchokela muukapolo wa kuwangika, ni kupachidwa ufulu wa ulemelelo wa wana a Mnungu.

Nambho saino mwalekeleledwa kuchokela ku ukapolo wa machimo, ni mwakhala akapolo a Mnungu, mwakhala wandhu wake ni mathelo yake simpate umoyo wa muyaya.

Nambho saino mwalekeleledwa kuchokela ku ukapolo wa machimo, ni mwakhala akapolo a Mnungu, mwakhala wandhu wake ni mathelo yake simpate umoyo wa muyaya.

Akapolo akuchita yayo yamkwadilicha Mnungu

Chipano tikambe chiyani? Tichite machimo ndande sitichogozedwa ni thauko nambho tichochogozwedwa ni ubwino? Notho!

Kuvomelezedwa kwa njila ya kukhulupilila

Nambho chipano njila ya kwachita wandhu avomelezeke kwa Mnungu ili padanga, popande kukhulupilila thauko, osati ngati umo lidakambila thauko la Musa ni malembo ya alosi a Mnungu vonjhe vikambilila chindhu chimenecho. Mnungu waavomela wandhu kuti ni woyela kwa njila ya chikhulupi chao kwa Yesu Kilisito, Mnungu wachita chimwecho kwa wonjhe akhulupilila, siwapatula Ayahudi ni wandhu yawo osati Ayahudi. Wandhu wonjhe achita machimo, palibe uyo wali wabwino ni wonjhe ataiza kulemekezedwa ni Mnungu. Nambho kwa mbhaso ya ubwino wa Mnungu, wandhu wonjhe avomelezedwa kuti ni abwino pachogolo pa Mnungu kwa njila ya Yesu Kilisito uyo wadaombola.

O Espírito liberta

Onde está o Espírito do Senhor, aí há liberdade. Olhe onde temos liberdade de acessar o trono da graça com confiança.

Yapa "Ambuye" nde Mzimu, ni yapo wali Mzimu wa Ambuye nde yapo pali ufulu.

Yapa "Ambuye" nde Mzimu, ni yapo wali Mzimu wa Ambuye nde yapo pali ufulu.

Chipano kwa kulunjana ni Kilisito ni kumkhulupilila, tipilila kumuwandikila Mnungu kwa kumkhulupilila.

"Mzimu wa Ambuye uli mkati mwanga,

pakuti wanisangha

kwaakambila wosauka uthenga wabwino.

Anituma kuti nauzile wandhu womangidwa ufulu wao,

ni wosapenya akhoze kuonanjho,

ni kwaapacha ufulu yawo aoneledwa.

"Mzimu wa Ambuye uli mkati mwanga,

pakuti wanisangha

kwaakambila wosauka uthenga wabwino.

Anituma kuti nauzile wandhu womangidwa ufulu wao,

ni wosapenya akhoze kuonanjho,

ni kwaapacha ufulu yawo aoneledwa.

Liberdade responsável

Fomos chamados à liberdade, mas não usemos a liberdade como pretexto para a carne. Tudo é lícito, mas nem tudo convém.

Pakuti anyiimwe mdatanidwa ni Mnungu dala mkale afulu, ufulu wanu usidakhala ndande yochata makumbilo ya thupi, nambho mfunika mtumikilane kwa chikondi.

Pakuti anyiimwe mdatanidwa ni Mnungu dala mkale afulu, ufulu wanu usidakhala ndande yochata makumbilo ya thupi, nambho mfunika mtumikilane kwa chikondi.

Tumilani Mathupi yanu kwa ulemelelo wa Mnungu

Mundhu siwakhoze kukamba, "Navomelezedwa kuchita chindhu chilichonjhe." Yetu, nambho osati kila vindhu vali vabwino kwaiwe. Nikhoza kukamba navomelezedwa kuchita chindhu chilichonjhe, nambho sinifuna kulamulidwa ni chindhu chalichonjhe.

A liberdade que permanece

Conhecer a verdade é o caminho da liberdade duradoura. Cristo nos resgatou e nos fez livres para viver em plenitude.

Chimwecho, achaabale wathu a Izilaeli mujhiwe kuti kwa njila ya Yesu, uthenga wa kulekeleledwa machimo ulalikidwa kwanu. Mundhu waliyonjhe uyo wamkhulupilila Kilisito siwalekeleledwe machimo yake. Chindhu icho sichidakakhozeka kwa kulemekeza thauko la Musa.

Chimwecho, achaabale wathu a Izilaeli mujhiwe kuti kwa njila ya Yesu, uthenga wa kulekeleledwa machimo ulalikidwa kwanu. Mundhu waliyonjhe uyo wamkhulupilila Kilisito siwalekeleledwe machimo yake. Chindhu icho sichidakakhozeka kwa kulemekeza thauko la Musa.

Yesu Mzabibu wa Uzene

Ndiipo Yesu wadakamba, "Ine ni mzabibu wa zene, ni Atate nde amlimi. Ndhawi yaliyonjhe iyo siibala vipacho mkati mwanga, Atate aidula, ni ndhawi iyo ibala aikonjezela ijhipunda kubala. Anyiimwe mwatho elechedwa muuzimu ndande ya uthenga uwo nidakuyaluzani. Khalani mkati mwanga, ngati umo ine nikhalila mkati mwanu. Ngati umo ndhawi ya mzabibibu siikhoza kubala yokha vipacho popande kukhala mumtengo wa mzabibu, chimwecho anyiimwe simukhoza kuchita chijha achifuna Amnungu ngati simukhala mkati mwanga."

"Ine ni mzabibu, anyiimwe ni ndhawi. Yao akhala mkati mwanga, nane nikakhala mkati mwao, achameneo sachite vindhu vabwino vambili, popande ine simukhoza kuchita kandhu. Mundhu wakasiya kukhala mkati mwanga wataidwa kubwalo ngati ndhawi ni kuuma. Ndhawi ngati zimenezo wandhu azikusa ni kuzitaya pamoto zipyelele. Anyiimwe mkakhala mkati mwanga ni mawu yanga yakakhala mkati mwanu, chipano, pembhani chilichonjhe icho mfuna namwe simpachidwe. Atate wanga apachidwa ulemelelo yapo mchita vindhu ivo vakwadilicha Amnungu, namwe simukhale oyaluzidwa wanga.

Seja o primeiro

Este artigo te tocou? Faça uma oração!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.