Pular para o conteúdo
Publicidade

Nascer de novo

Por Bíblia Online

Nascer de novo é a porta de entrada para a vida em Deus. Jesus ensinou que sem o novo nascimento espiritual, ninguém pode ver nem entrar no Reino de Deus.

A necessidade do novo nascimento

Jesus declarou a Nicodemos: 'Aquele que não nascer de novo não pode ver o Reino de Deus.' O novo nascimento é pelo Espírito.

Yesu wadamuyangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kakawili siwakhoza kuuona Ufumu wa Amnungu."

Yesu wadamuyangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kakawili siwakhoza kuuona Ufumu wa Amnungu."

Ndiipo Nikodemo wadamfunjha, "Mzee wakhoza bwanji kubadwanjho? Siwakhoze bwanji kulowa mmimba mwa amaye wake nikubaadwanjho?"

Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu Mundhu wabadwa chithupi kwa atate wake ni amake, nambho wabadwa Chizimu kwa Mzimu woyela. Siudadabwa pakuti nakukambila kuti lazima kubadwanjho. Mbhepo iputa ni kupita uko ifuna, uvela mvekelo wake, nambho siujhiwa uko ichoka kapina uko ipita. Nde umo ili kwa mundhu uyo wabadwa kwa Mzimu woyela."

Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu Mundhu wabadwa chithupi kwa atate wake ni amake, nambho wabadwa Chizimu kwa Mzimu woyela. Siudadabwa pakuti nakukambila kuti lazima kubadwanjho.

Zenedi nikukambilani, mundhu waliyonjhe uyo siwaulandila Ufumu wa Mnungu ngati wana wang’onoangono umo aulandilila, siwalowelatu muufumu wa Mnungu."

Yani waliwamkulu pa Ufumu wa Mnungu

Ndhawi imeneyo oyaluzidwa adamchata Yesu, adaamfunjha, "Yani uyo wali wamkulu kupitilila wonjhe mu Ufumu wa kumwamba?"

Yesu wadamtana mwana wamng’ono ni kumwimika pakati pao, Ndiipo wadaakambila, "Zene nikukambilani, ngati simng’anamuka ni kulingana ni wana waang’onoangono, simulowa mu Ufumu wa kumwamba. Waliyonjhe uyo wajhichepecha ngati mwana uyu, nde uyo siwakhale wamkulu mu Ufumu wa kumwamba.

Nova criação em Cristo

Quem está em Cristo é nova criação. Morremos e ressuscitamos com Ele para viver em novidade de vida, livres do velho homem.

Chimwecho mundhu waliyonjhe wakalunjana ni Kilisito, wakhala mundhu wa chipano, yakale yatha, yakhala yachipano.

Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.

Pakuti ife talunjana niiye kwa njila nyifa yake, chimwecho ife sitilunjane naye kwa kuhyukichidwa ngati iye. Tijhiwa kuti vichito vathu va kale vidafa ni vidapachikidwa pa mtanda pamojhi niiye, kuti mbhavu za machimo ziwanangidwe, ni sitidakhalanjho akapolo a machimo. Mundhu wakafa kwa mtundu umeneo siwakhaliletu hulu kuchokela mmbhavu za machimo.

Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.

Chinchijha anyiimwe ifunika mjhione kuti mwafa kwa nghani ya machimo, nambho ngati mkhala kwa umojhi ni Mnungu kwa kumkhulupilila Yesu Kilisito.

nisaino nikhala wamoyo, nambho asati inenjho, nambho ni Kilisito wakhala mkati mwanga, ukhalo uno nikhala saino nikhala kwa kukhulupilila. Kukhulupilila kwanga kuchokana ni Mwana wa Mnungu, uyo wadanikonda ni wadauchocha umoyo wake ndande yanga.

Mudayaluzidwa muvisiye vichito vanu voipa ivo madavichita kale, ngati mujha mundhu wavulila njalu ni kuisiya, vichito ivo vimawanangidwa ni khumbilo launami. Mmizimu mwanu ni mmaganizo yanu mving’anamule vikhale va chipano. Mkhale ni umoyo wa chipano, ngati umo mmungu wadakuumbani, mlingane niiye uku muli ovomelezeka kupunda ni kukhala umo ifunukila.

Filhos de Deus

Nascemos de novo pela Palavra viva de Deus. Quem crê em Jesus recebe o direito de se tornar filho de Deus, nascido do Espírito.

Nambho anyiyawo adamlandila, nikumkhulupilila mwadapacha nghongono za kukhala wana Amnungu, nde anyiwajha alikhulupilila jhina lawo, anyiyawo abadwa asati kwa mwazi, kapina kwa kukonda kwa thupi au kukonda kwa mundhu, nambho Amnungu nde yawo adali Atate wao.

Nambho ndhawi yeneyene yapo idakwana Amnungu adamtuma Mwana wao uyo pajhiko lino la panjhi. Mwana uyo wadabadwa ni wamkazi, mwana mmeneyo wadachgozedwa ni thauko la Musa, waombole anyiwajha achogozedwa ni thauko, dala ife Ayahudi tichitidwe kukhala wana Amnungu.

Nambho Mnungu ni alisungu kupunda. Adatikonda kwa chikondi chachikulu, ata ngati tidamwalila ndande ya machimo, adatichita amoyo pamojhi ni Kilisito. Kwa ubwino wa Mnungu anyiimwe mwaomboledwa.

Seja o primeiro