Pular para o conteúdo
Publicidade

Afilipi 4:6-9

NTNYBL2025 Nyanja

6 Msadachita mandha pa chindhu chalichonjhe, nambho pa kila chindhu, pa kwapembha Mnungu mwa mayamiko, ni mapembhelo yanu siya jhuwike. 7 Ni mtendele wa Amnungu, upitilila njelu zonjhe, zikusungeni mitima yanu, ni njelu zanu, mwa Kilisito Yesu.

8 Potela mpenye vindhu vazene, ni yamate, yavomeleka, yaelecheka, yakhadwa ni yaulemu. 9 Vindhu vonjhe mwajiyaluza kwanga kapina kuyalandila kapina kuyavela kapina kuyaona, yachiteni yameneyo. Ni Mnungu watupacha mtendele siwakhale pamojhi nianyiimwe.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    6 Musade nkhawa ndi kanthu kalikonse, koma pa china chilichonse, mwa pemphero ndi chidandaulo pamodzi ndi chiyamiko, perekani zopempha zanu kwa Mulungu. 7 Ndipo mtendere wa Mulungu, umene upambana nzeru zonse udzasunga bwino mitima yanu ndi maganizo anu mwa Khristu Yesu.

    8 Potsiriza, abale, muziyika mtima wanu pa zinthu zilizonse zabwino ndi zotamandika monga, zinthu zoona, zinthu zolemekezeka, zinthu zolungama, zinthu zoyera, zinthu zokongola ndi zinthu zosiririka. 9 Muzichita chilichonse chimene mwaphunzira kapena kulandira kapena kumva kuchokera kwa ine kapena mwaona mwa ine. Ndipo Mulungu wamtendere adzakhala nanu.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Filipenses
Ver todos os capítulos de Filipenses