Pular para o conteúdo
Publicidade

Resultados da busca por "salvação"

57 resultados encontrados

  1. Lucas 24

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 24
    Mostrando versículos 2–51 de 53

    2Anaona mwala wa pa manda utagubuduzika

    6Iye sali muno ayi. Wauka! Kumbukirani zimene anakuwuzani pamene anali nanu ku Galileya:

    51Iye akuwadalitsa, anawasiya ndipo anatengedwa kupita kumwamba.

  2. Jó 31

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 31
    Mostrando versículos 2–33 de 40

    2Kodi Mulungu kumwambako wandisungira zotani?Kodi cholowa changa chochokera kwa Wamphamvuzonse kumwambako nʼchotani?

    12Ndi moto umene umayaka mpaka chiwonongeko;ukanapsereza zokolola zanga.

    33ngati ndinabisa tchimo langa monga amachitira anthu ena,kubisa kulakwa mu mtima mwanga

  3. Provérbios 18

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 18
    Mostrando versículos 10–18 de 24

    10Dzina la Yehova lili ngati nsanja yolimba;wolungama amathawiramo napulumuka.

    16Mphatso ya munthu imamutsekulira njirayomufikitsa pamaso pa anthu akuluakulu.

    18Kuchita maere kumathetsa mikangano;amalekanitsa okangana amphamvu.

  4. Números 7

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 7
    Mostrando versículos 28–52 de 89

    28mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;

    34mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;

    52mbuzi imodzi ya nsembe yopepesera machimo;

  5. Isaías 36

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 36
    Mostrando versículos 18–20 de 22

    18"Inu musalole kuti Hezekiya akusocheretseni pamene iye akuti, ‘Yehova adzatipulumutsa.’ Kodi alipo mulungu wa anthu a mtundu wina amene anapulumutsa dziko lake mʼdzanja la mfumu ya ku Asiriya?

    19Kodi ili kuti milungu ya Hamati ndi Aripadi? Ili kuti milungu ya Sefaravaimu? Kodi inapulumutsa Samariya mʼdzanja langa?

    20Kodi ndi milungu iti mwa milungu yonse ya mayiko awa amene anapulumutsa dziko lake mʼdzanja? Nanga tsono Yehova adzapulumutsa Yerusalemu mʼdzanja langa motani?"

  6. Salmos 76

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 76
    Mostrando versículos 2–9 de 12

    2Tenti yake ili mu Salemu,malo ake okhalamo mu Ziyoni.

    7Inu nokha ndiye muyenera kuopedwa.Angathe kuyima pamaso panu ndani mukakwiya?

    9pamene Inu Mulungu munadzuka kuti muweruze,kupulumutsa onse osautsidwa mʼdziko.Sela

  7. Provérbios 29

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 29
    Mostrando versículos 5–23 de 27

    5Munthu woshashalika mnzake,akudziyalira ukonde mapazi ake.

    10Anthu okhetsa magazi amadana ndi munthu wangwirokoma anthu olungama amasamalira moyo wake.

    23Kunyada kwa munthu kudzamutsitsa,koma munthu wodzichepetsa amalandira ulemu.

  8. Salmos 18

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 18
    Mostrando versículos 2–46 de 50

    2Yehova ndiye thanthwe langa, chitetezo changa ndi mpulumutsi wanga;Mulungu wanga ndi thanthwe langa mʼmene ndimathawiramo.Chishango changa ndi ndodo yachipulumutso changa, ndi linga langa.

    27Inu mumapulumutsa anthu odzichepetsa,koma anthu amtima odzikuza mumawatsitsa.

    46Yehova ndi wamoyo! Litamandidwe Thanthwe langa!Akuzike Mulungu Mpulumutsi wanga!

  9. Salmos 62

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 62
    Mostrando versículos 1–8 de 12

    1Moyo wanga umapeza mpumulo mwa Mulungu yekha;chipulumutso changa chimachokera kwa Iye.

    3Kodi nonsenu mudzalimbana naye munthu mpaka liti?Kodi mudzamugwetsa pansi ngati khoma losalimba,ngati mpanda wogwedezeka?

    8Dalirani Iye nthawi zonse, inu anthu;khuthulani mitima yanu kwa Iye,pakuti Mulungu ndiye pothawirapo pathu.Sela

  10. Salmos 85

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 85
    Mostrando versículos 2–7 de 13

    2Munakhululukira mphulupulu za anthu anundi kuphimba machimo awo onse.Sela

    5Kodi mudzatikwiyira mpaka liti?Kodi mudzapitiriza kukwiya pa mibado yathu yonse?

    7Tionetseni chikondi chanu chosatha, Inu Yehova,ndipo tipatseni chipulumutso chanu.

  11. Salmos 147

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 147
    Mostrando versículos 1–16 de 20

    1Tamandani Yehova.Nʼkwabwino kwambiri kuyimba nyimbo zamatamando kwa Mulungu wathu,nʼkokondweretsa ndi koyenera kumutamanda!

    3Akutsogolera anthu osweka mtimandi kumanga mabala awo.

    16Amagwetsa chisanu ngati ubweyandi kumwaza chipale ngati phulusa.

  12. Salmos 84

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 84
    Mostrando versículos 1–8 de 12

    1Malo anu okhalamo ndi okomadi,Inu Yehova Wamphamvuzonse!

    4Odala amene amakhala mʼNyumba yanu;nthawi zonse amakutamandani.Sela

    8Imvani pemphero langa, Inu Yehova Mulungu Wamphamvuzonse;mvereni Inu Mulungu wa Yakobo.Sela

  13. Salmos 7

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 7
    Mostrando versículos 6–10 de 17

    6Nyamukani Yehova, mu mkwiyo wanu;nyamukani kutsutsana ndi mkwiyo wa adani anga.Dzukani Mulungu wanga, lamulirani chilungamo chanu.

    7Lolani gulu la anthu a mitundu ina lisonkhane mokuzungulirani.Alamulireni muli kumwambako;

    10Chishango changa ndi Mulungu Wammwambamwamba,amene amapulumutsa olungama mtima.

  14. Salmos 150

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 150
    Mostrando versículos 1–6 de 6

    1Tamandani Yehova.Tamandani Mulungu mʼmalo ake opatulika;mutamandeni ku thambo lake lamphamvu.

    3Mutamandeni poyimba malipenga,mutamandeni ndi pangwe ndi zeze.

    6Chamoyo chilichonse chopuma chitamande Yehova.Tamandani Yehova.

  15. Salmos 80

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 80
    Mostrando versículos 2–19 de 19

    2kwa Efereimu, Benjamini ndi Manase.Utsani mphamvu yanu;bwerani ndi kutipulumutsa.

    15muzu umene dzanja lanu lamanja ladzala,mwana amene inu munamukuza nokha.

    19Tibwezereni mwakale Inu Yehova Mulungu Wamphamvuzonsenkhope yanu itiwalirekuti tipulumutsidwe.

  16. Salmos 116

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 116
    Mostrando versículos 6–15 de 19

    6Yehova amateteza munthu wodzichepetsa mtima;pamene ndinali ndi chosowa chachikulu, Iye anandipulumutsa.

    13Ndidzakweza chikho cha chipulumutsondipo ndidzayitana dzina la Yehova.

    15Imfa ya anthu oyera mtimandi yamtengowapatali pamaso pa Yehova.

  17. Salmos 28

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 28
    Mostrando versículos 6–8 de 9

    6Matamando apite kwa Yehova,popeza Iye wamva kupempha chifundo kwanga.

    7Yehova ndiye mphamvu yanga ndi chishango changa;mtima wanga umadalira Iye, ndipo Ine ndathandizidwa.Mtima wanga umalumphalumpha chifukwa cha chimwemwendipo ndidzayamika Iye mʼnyimbo.

    8Yehova ndi mphamvu ya anthu ake,linga la chipulumutso kwa wodzozedwa wake.

Léxico (correspondência exata) Semântico (correspondência relacionada) Versículos omitidos Contexto do capítulo