Pular para o conteúdo
Publicidade

Resultados da busca por "amor"

24 resultados encontrados

  1. Provérbios 27

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 27
    Mostrando versículos 5–15 de 27

    5Kudzudzula munthu poyera nʼkwabwinokuposa chikondi chobisika.

    13Utenge chovala cha munthu amene waperekera mlendo chikole;ngati chigwiriro chifukwa waperekera chikole mlendo wosadziwika.

    15Mkazi wolongolola ali ngatimvula yamvumbi.

  2. 1 Crônicas 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículo 14 de 54

    14Ayebusi, Aamori, Agirigasi

  3. Romanos 12

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 12
    Mostrando versículos 9–15 de 21

    9Chikondi chikhale chopanda chinyengo. Dana nacho choyipa; gwiritsitsa chabwino.

    10Mukondane kwathunthu monga abale. Lemekezanani wina ndi mnzake kuposa inu eni.

    15Kondwani pamodzi ndi amene akukondwa ndipo lirani ndi amene akulira.

  4. Provérbios 29

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 29
    Mostrando versículos 5–22 de 27

    5Munthu woshashalika mnzake,akudziyalira ukonde mapazi ake.

    17Umulange mwana wako ndipo adzakupatsa mtenderendi kusangalatsa mtima wako.

    22Munthu wamkwiyo amayambitsa mikangano,ndipo munthu waukali amachita zolakwa zambiri.

  5. Salmos 136

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 136
    Mostrando versículo 19 de 26

    19Siloni mfumu ya Aamori,pakuti chikondi chake chosasinthika nʼchamuyaya.

  6. 1 Coríntios 13

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 13
    Mostrando versículos 4–8 de 13

    4Chikondi nʼcholeza mtima, chikondi nʼchokoma mtima, chilibe nsanje, sichidzikuza, sichidzitamandira.

    5Chikondi chilibe mwano, sichodzikonda, sichipsa mtima msanga, sichisunga mangawa.

    8Chikondi ndi chosatha. Koma mphatso ya uneneri idzatha, pamene pali kuyankhula malilime adzatha, pamene pali chidziwitso chidzatha.

  7. João 15

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 15
    Mostrando versículos 12–17 de 27

    12Lamulo langa ndi ili: ‘Kondanani wina ndi mnzake monga Ine ndakonda inu.’

    13Palibe munthu ali ndi chikondi choposa ichi, choti munthu nʼkutaya moyo wake chifukwa cha abwenzi ake.

    17Lamulo langa ndi ili: ‘Muzikondana.’

  8. 1 Timóteo 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 5–18 de 20

    5Cholinga cha lamuloli ndi chikondi, chomwe chimachokera mu mtima woyera, chikumbumtima chabwino ndi chikhulupiriro choona.

    17Tsopano kwa Mfumu yamuyaya, yosafa, yosaoneka, amene Iye yekha ndiye Mulungu, kukhale ulemu ndi ulemerero mpaka muyaya. Ameni.

    18Mwana wanga Timoteyo, ndikukupatsa langizo ili molingana ndi maulosi amene aneneri ananena za iwe. Pamene ukumbukira mawu amenewa udzatha kumenya bwino nkhondo

  9. 1 Coríntios 16

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 16
    Mostrando versículos 14–24 de 24

    14Chitani zonse mwachikondi.

    20Abale onse kuno akupereka moni wawo. Patsanani moni wachikondi chenicheni.

    24Chikondi changa chikhale ndi nonsenu mwa Khristu Yesu.

  10. Ezequiel 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 14–19 de 28

    14Zamoyozo zinkathamanga uku ndi uko ngati kungʼanima kwa mphenzi.

    17Mikombero ija poyenda inkatha kupita mbali iliyonse yomwe zamoyozo zinayangʼana popanda kutembenuka.

    19Zamoyozo zinkati zikamayenda, mikomberoyo imayendanso mʼmbali mwake; ndipo zamoyozo zinkati zikamakwera mmwamba, mikomberoyo imakweranso.

  11. 1 Pedro 4

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 4
    Mostrando versículos 8–12 de 19

    8Koposa zonse muzikondana wina ndi mnzake kwambiri, chifukwa chikondi chimaphimba machimo ambiri.

    9Muzisamalirana wina ndi mnzake osamanyinyirika.

    12Abale okondedwa musadabwe ndi mayesero owawa amene mukukumana nawo ngati kuti china chake chachilendo chakuchitikirani.

  12. Romanos 16

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 16
    Mostrando versículos 8–24 de 27

    8Perekani moni kwa Ampliato, amene ine ndimamukonda mwa Ambuye.

    16Mupatsane moni wina ndi mnzake mwachikondi choona.Mipingo yonse ya Khristu ikupereka moni.

    24Chisomo cha Ambuye athu Yesu Khristu chikhale ndi inu nonse. Ameni.

  13. Jó 18

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 18
    Mostrando versículos 8–16 de 21

    8Mapazi ake amulowetsa mu ukondendipo akungoyendayenda mu ukondewo.

    10Amutchera msampha pansi mobisika;atchera diwa pa njira yake.

    16Mizu yake ikuwuma pansindipo nthambi zake zikufota

  14. 2 Coríntios 6

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 6
    Mostrando versículos 6–11 de 18

    6pokhala moyo woyera mtima, pomvetsa zinthu, wokoma mtima ndi wachifundo mwa Mzimu Woyera ndi mwachikondi choonadi

    7ndi poyankhula choonadi mwamphamvu ya Mulungu. Zida zimene zili mʼdzanja lamanja ndi lamanzere ndizo chilungamo.

    11Tayankhula momasuka kwa inu, Akorinto, ndipo tanena zonse za kumtima kwathu.

  15. Cânticos 6

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 6
    Mostrando versículos 1–10 de 13

    1Iwe wokongola kuposa akazi onsewa,kodi wokondedwa wakoyo wapita kuti?Kodi wokondedwa wakoyo wakhotera njira itikuti timufunefune pamodzi ndi iwe?Mkazi

    3Wokondedwa wangayo ndine wake ndipo iyeyo ndi wangawanga;amadyetsa ziweto zake pakati pa maluwa okongola.Mwamuna

    10Ndani uyu akuoneka ngati mʼbandakucha,wokongola ngati mwezi, wowala ngati dzuwa,wochititsa mantha ngati gulu la ankhondo mbendera zili mʼmanja?Mwamuna

  16. Salmos 150

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 150
    Mostrando versículos 1–6 de 6

    1Tamandani Yehova.Tamandani Mulungu mʼmalo ake opatulika;mutamandeni ku thambo lake lamphamvu.

    3Mutamandeni poyimba malipenga,mutamandeni ndi pangwe ndi zeze.

    6Chamoyo chilichonse chopuma chitamande Yehova.Tamandani Yehova.

  17. Cânticos 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 2–14 de 17

    2Undipsompsone ndi milomo yakochifukwa chikondi chako nʼchokoma kuposa vinyo.

    13Wokondedwa wanga ali ngati kathumba ka mure kwa ine,kamene kamakhala pakati pa mawere angawa.

    14Wokondedwa wanga ali ngati mpukutu wa maluwa ofiira,ochokera ku minda ya mpesa ya ku Eni-Gedi.Mwamuna

  18. Gálatas 1

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 1
    Mostrando versículos 5–11 de 24

    5Ulemerero ukhale kwa Mulunguyo mpaka muyaya. Ameni.

    7umene si Uthenga Wabwino konse. Pali anthu ena amene akukusokonezani komanso akufuna kupotoza Uthenga Wabwino wa Khristu.

    11Abale, ine ndikufuna kuti mudziwe, kuti Uthenga Wabwino umene ndinalalikira si ochokera kwa munthu ayi.

  19. Mateus 24

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 24
    Mostrando versículos 8–18 de 51

    8Zonsezi ndi chiyambi chabe cha zowawa.

    12Chifukwa cha kuchuluka kwa zoyipa, chikondi cha ambiri chidzazirala,

    18Yemwe ali ku munda asapite kukatenga mkanjo wake.

  20. Números 26

    Tsekulani Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero
    Capítulo 26
    Mostrando versículos 6–59 de 65

    6kuchokera mwa Hezironi, fuko la Ahezironi;kuchokera mwa Karimi, fuko la Akarimi.

    55Dzikolo uligawe pochita maere. Alandire cholowa chawocho potsata mayina a mafuko a makolo awo.

    59Dzina la mkazi wa Amramu linali Yokobedi, mdzukulu wa Levi, yemwe anabadwa mwa Alevi mu Igupto. Yokobedi anaberekera Amramu Aaroni, Mose ndi Miriamu mlongo wawo.

Léxico (correspondência exata) Semântico (correspondência relacionada) Versículos omitidos Contexto do capítulo