Pular para o conteúdo
Publicidade

YEREMIYA 1

6 Ine ndinati, "Haa! Ambuye Yehova, ine sinditha kuyankhula; popeza ndikanali wamngʼono."

7 Koma Yehova anandiwuza kuti, "Usanene kuti, Ndikanali wamngʼonopopeza udzapita kwa munthu aliyense kumene ndidzakutuma ndi kunena chilichonse chimene ndidzakulamulira. 8 Usawaope, pakuti Ine ndili nawe, ndipo ndidzakupulumutsa," akutero Yehova.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também