7 Koma Yehova anandiwuza kuti, "Usanene kuti, ‘Ndikanali wamngʼono’ popeza udzapita kwa munthu aliyense kumene ndidzakutuma ndi kunena chilichonse chimene ndidzakulamulira. 8 Usawaope, pakuti Ine ndili nawe, ndipo ndidzakupulumutsa," akutero Yehova.
Publicidade
Publicidade