Pular para o conteúdo
Publicidade

YEREMIYA 3

14 "Bwererani, ana osakhulupirika, pakuti ndine mbuye wanu," akutero Yehova. "Ndinakusankhani, mmodzimmodzi kuchokera ku mudzi uliwonse ndiponso awiriawiri kuchokera ku banja lililonse. 15 Ndipo ndidzakupatsani abusa a pamtima panga amene adzakutsogolerani mwanzeru ndi mwaluntha. 16 Masiku amenewo mukadzachulukana kwambiri mʼdzikomo, anthu sadzanenanso za Bokosi la Chipangano la Yehovakapena kuliganizira. Sadzalikumbukiranso kapena kulifuna, ndipo sadzapanganso lina,"

akutero Yehova.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também