15 Yehova akuti,
"Kulira kukumveka ku Rama,
kulira kwakukulu,
Rakele akulirira ana ake.
Sakutonthozeka
chifukwa ana akewo palibe."
15 Yehova akuti,
"Kulira kukumveka ku Rama,
kulira kwakukulu,
Rakele akulirira ana ake.
Sakutonthozeka
chifukwa ana akewo palibe."