Pular para o conteúdo
Publicidade

YEREMIYA 9

23 Yehova akuti,

"Munthu wanzeru asanyadire nzeru zake,

kapena munthu wamphamvu kunyadira nyonga zake,

kapena munthu wolemera kunyadira chuma chake,

24 koma ngati munthu akufuna kunyadira, anyadire chinthu ichi:

kuti iye amamvetsa za Ine ndipo amandidziwa,

kuti ndine Yehova, amene ndimakonda chifundo,

chilungamo ndiponso ungwiro pa dziko lapansi.

Zimenezi ndizo ndimakondwera nazo,"

akutero Yehova.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também