Pular para o conteúdo
Publicidade

YOBU 2

9 Mkazi wake anati kwa iye, "Kodi ukuwumirirabe kukhala wangwiro? Tukwana Mulungu kuti ufe!"

10 Yobu anayankha kuti, "Ukuyankhula ngati mkazi wopusa. Kodi tidzalandira zokoma zokhazokha kwa Mulungu, osalandiranso zowawa?"

Mu zonsezi, Yobu sanachimwe pa zimene anayankhula.

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Veja também