Pular para o conteúdo
Publicidade

O adultério

Por Bíblia Online

O adultério é pecado grave que destrói alianças, famílias e vidas. A Bíblia condena firmemente a infidelidade conjugal e chama à pureza, fidelidade e santidade no casamento.

A lei de Deus

Não adulterarás. Quem comete adultério destrói a própria alma. A Palavra de Deus é clara e direta sobre este pecado.

Jesus ensina

Quem olhar para uma mulher com intenção impura já adulterou no coração. Jesus elevou o padrão da pureza.

Mayaluzo kuusu chigololo

Yesu wadaendekela kukamba, "Mwavela kuti wandhu adakambilidwa, Usadachita chigololo!Nambho ine nikukambilani kuti uyo siwampenye wamkazi kwa kumkhumbila wathochita chigololo mumtima mwake.

Nambho ine nikukambilani mundhu waliyonjhe uyo siwamsiye mkazake kwa ndande yaliyonjhe ijha ni osati kwa ndande ya chigololo wamchita mkazake kukhala wachigololo, ni wammuna waliyonjhe uyo siwamkwate wamkazi uyo wasiidwa nayo wachita chigololo."

Pakuti mumtima yachoka maganizo ya kupha, chigololo, uhule, unami, kuba, umboni wanthila ni matukwano.

Yesu wadaakambila, "Wammuna waliyonjhe uyo wamsiya wamkazi ni kukwata mwina, wamchitila chigololo mkazake. Chinchijha, wamkazi wakamsiya mmunake ni kupita kukwatiwa ni wammuna mwina, wamchitila chigololo mmunake."

Waliyonjhe uyo wamsiya mkazake ni kukwata wamkazi mwina, wachita chogololo. Ni wammuna uyo wamkwata wamkazi uyo wasiyidwa ni mmunake, wachitanayo chigololo.

Ndiipo adamfunjha Yesu, "Oyaluza, wamkazi uyu wagwilidwa ni wachita chigololo. Muthauko, Musa wadatilamula wamkazi ngati uyu wabulidwe miyala mpaka kumwalila. Imwe mkamba bwanji?" Adamuyesa kokamba chimwecho, kuti ampache mlandu. Nambho Yesu wadakwatama panjhi ni kulemba pa ndhaka kwa chala chake.

Yapo adapunda kumfunjha, wadaima nikwakambila, "Mundhu waliyonjhe uyo walibe machimo pakati panu wakhale oyamba kumbula mwala." Wadakwatamanjho ni kulemba pandhaka kwa chala chake. Yapo adavela chimwecho adayamba kuchoka mmojhimmojhi, adachogola azee. Wadakhalila Yesu yokha ni wamkazi waima pachogolo pake. Yesu yapo wadaima wadamfunjha wamkaziyo, "Alikuti wajha wandhu akupacha mlandhu? Palibe waliyonjhe uyo wakulamula?"

Wamkazi mmeneyo wadayangha, "Wakulu, palibe waliyonjhe!"

Ndiipo Yesu wadamkambila, "Ata ine sinikulamula. Mapita siudachitanjho machimo."

Armadilhas e consequências

Os lábios da mulher estranha destilam mel, mas o seu fim é amargo. Fuja da imoralidade — o adultério escraviza.

Chithaweni chigololo. Machimo yina yonjhe wachita mundhu wachita kubwalo kwa thupi lake, nambho mundhu uyo wachita chigololo wachita mkhati mwathupi lake mwene wake.

Kuchogozedwa ni Mzimu wa Mnungu

Chipano nikamba chimwechi, ukhalo wanu uchogozedwe ni Mzimu wa Mnungu, mkachita chimwecho simuchatanjho makumbilo yoipa. Pakuti makhumbolo yoipa yachuchana ni makhumbilo ya Mzimu wa Mnungu, nayo Mzimu wa Mnungu siwakhumbila vindhu voipa. Vindhu vimenevo vichuchana, ndande imeneyo simkhoza kuchita yayo mfuna.

Vichito va jhiko vijhiwika navo nde ivi, uhule, chigololo, ni ukhalo woyipa, kulambila viboliboli, ufiti, udani, ndewo, njhanje, mbwayi, chipili, mkangano ni kosavana, kosakondwela mwina wakakhala ni chindhu, kulojhela mowa kudya kupunda ni vindhu vili ngati vimenevo. Nikuonyani ngati umo nidakuonyelani mmayambo, wandhu achita yameneyo saupata ufumu wa Amnungu.

Seja o primeiro