Pular para o conteúdo
Publicidade

O Espírito Santo

Por Bíblia Online

O Espírito Santo é a terceira pessoa da Trindade — Consolador, Mestre e Poder. Ele convence do pecado, guia em toda verdade, distribui dons e produz frutos na vida do cristão.

O Consolador prometido

Jesus prometeu enviar o Consolador — o Espírito da Verdade — que estaria para sempre com os discípulos e os guiaria em toda verdade.

Sinaapembhe Atate nawo sakupacheni Wakukuthandizani mwina, uyo siwakhale namwe muyaya.

Sinaapembhe Atate nawo sakupacheni Wakukuthandizani mwina, uyo siwakhale namwe muyaya. Iye ni Mzimu wa zene. Jhiko lapanjhi silikhoza kumlandila ndande silimuona kapina kumjhiwa. Nambho anyiimwe mumjhiwa ndande wakhala namwe ni wali mkati mwanu."

"Sinikusiyani amasiye, sinijhenjho kwanu. Ikali ndhawi yochepa wandhu ajhiko la panjhi sanionanjho, nambho anyiimwe simunione, pakuti ine nili wamoyo namwenjho simukhale moyo. Ndhawi ijha ikafika simujhiwe kuti ine nilimkati mwa Atate, namwe muli mkati mwanga ni ine nilimkati mwanu."

"Uyo wayalandila malamulo yanga ni kuyagwila, mmeneyo nde uyo wanikonda. Uyo wanikonda ine siwakondedwe ni Atate wanga, nane sinimkonde ni kujhijhiwicha kwa iye."

Chimwecho Yuda nambho osati Isikaliyote adamkambila, "Ambuye, sikhozeke bwanji mujhilangize kwa ife ni osati kwa jhiko?"

Yesu wadayangha, "Wandhu yao anikonda akalichitila njhito mawu langa ni Atate wanga saakonde, nafe sitijhe kwa anyiiwo ni kukhala pamojhi nawo. Uyo siwanikonda siwayachitila njhito mawu yanga. Uthenga uwo muuvela osati wanga nambho uchokela kwa Atate yao anituma."

"Nikuyaluzani vindhu ivi nikali pamojhi namwe, nambho Othandiza, Mzimu woyela, uyo samtume kukhala mmalo mwanga, siwakuyaluzeni kila kandhu ni kukukumbuchani yonjhe yayo nakukambilani."

nambho Othandiza, Mzimu woyela, uyo samtume kukhala mmalo mwanga, siwakuyaluzeni kila kandhu ni kukukumbuchani yonjhe yayo nakukambilani."

nambho Othandiza, Mzimu woyela, uyo samtume kukhala mmalo mwanga, siwakuyaluzeni kila kandhu ni kukukumbuchani yonjhe yayo nakukambilani."

"Yapo siwajhe othandiza uyo sinimtume kuchoka kwa Atate, Mzimu wauzene uyo wachokela kwa Atate, siwanichochele umboni.

Nambho nikukambilani uzene, mbasa ine nipite, mate yake nikasiya kupita Othandiza siwajha kwanu. Nambho nikapita, sinimtume kwanu. Nayo yapo siwajhe siwachimikizile wandhu ajhiko nghani za machimo, kuvomelezeka ni lamulo la Amnungu.

Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu

Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu Mundhu wabadwa chithupi kwa atate wake ni amake, nambho wabadwa Chizimu kwa Mzimu woyela. Siudadabwa pakuti nakukambila kuti lazima kubadwanjho.

Ine sinimamjhiwe, nambho uyo wanituma kubatiza wandhu kwa majhi wanikambila, Mundhu uyo siwauone mzimu niuchika kuchoka kumwamba ni kukhala pa mwamba pake, nde uyo wabatiza kwa Mzimu Woyela.

O derramamento do Espírito

No Pentecostes, o Espírito desceu como fogo sobre os discípulos. Desde então, todos os que creem recebem o Espírito.

Kujha kwa Mzimu Woyela

Yapo lidafika siku la pwando la Pentekosite, wandhu wonjhe yawo adamkhulupilila Yesu adasonghana malo yamojhi. Mwachizulumukila mvekelo waukulu ngati mkokomo wa mbhepo udachoka kumwamba ni kuijhaza nyumba yonjhe mujha adakhala wajha atumwi. Kudatulukila malilime ya moto yayo yadagawika ni kukhala pamwamba pa kila mmojhi wawo. Wandhu wonjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela, adayamba kukamba mikambo ya chilendo, ngati umo wadafunila Mzimu Woyela.

Ndiipo kudali Ayahudi yawo amakhala mu Yelusalemu, yawo adachokela ku maiko yonjhe ya pajhiko lapanjhi.

Mwachizulumukila mvekelo waukulu ngati mkokomo wa mbhepo udachoka kumwamba ni kuijhaza nyumba yonjhe mujha adakhala wajha atumwi. Kudatulukila malilime ya moto yayo yadagawika ni kukhala pamwamba pa kila mmojhi wawo. Wandhu wonjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela, adayamba kukamba mikambo ya chilendo, ngati umo wadafunila Mzimu Woyela.

Kudatulukila malilime ya moto yayo yadagawika ni kukhala pamwamba pa kila mmojhi wawo. Wandhu wonjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela, adayamba kukamba mikambo ya chilendo, ngati umo wadafunila Mzimu Woyela.

Petulo wadaayangha, "Lapani, kila mmojhi wanu mmbatizidwe kwa jhila la Yesu Kilisito, kuti mlekeleledwe machimo yanu ni kulandila ahadi ijha ya Mzimu Woyela.

Petulo wadaayangha, "Lapani, kila mmojhi wanu mmbatizidwe kwa jhila la Yesu Kilisito, kuti mlekeleledwe machimo yanu ni kulandila ahadi ijha ya Mzimu Woyela.

Nambho simujhazidwe mbhavu yapo siwajhe kwanu Mzimu woyela, ni anyiimwe simukhale amboni wanga mmijhi ya Yelusalemu, Yudea yonjhe ni Samaliya, ni jhiko lonjhe lapanjhi."

Nambho simujhazidwe mbhavu yapo siwajhe kwanu Mzimu woyela, ni anyiimwe simukhale amboni wanga mmijhi ya Yelusalemu, Yudea yonjhe ni Samaliya, ni jhiko lonjhe lapanjhi."

Yapo adangomaliza kupembhela, pamalo pajha adakomanilana padatingizika. Wandhu onjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela ni kukamba mau la Mnungu popande mandha.

Yapo adangomaliza kupembhela, pamalo pajha adakomanilana padatingizika. Wandhu onjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela ni kukamba mau la Mnungu popande mandha.

Ife ni amboni a nghani zimenezo, chinchijha ata Mzimu Woyela uyo Mnungu waapacha wandhu wajha amvela wachimikiza chindhu chimenecho."

Yapo amampembha Mnungu ni kumanga kudya, Mzimu Woyela udaakambila, "Nipatulileni Banaba ni Saulo, kuti achite njhito iyo naatanila kuchita."

Ochatila achameneo yapo adavela chimwecho, adabatizidwa mujhina la Ambuye Yesu. Poolo wadaasanjika manja, ni Mzimu Woyela adachikila anyiiwo, ni kuyamba kukamba mikambo yachilendo ni adayamba kuuzila Uthenga wa Mnungu.

Dons do Espírito

A cada um é concedida a manifestação do Espírito para o bem de todos. Os dons são diversos, mas o Espírito é o mesmo.

Nambho, mbhaso za muuzimu apachidwa wandhu osiyanasiyana dala za thangatile wandhu wina. Mzimu umpacha mundhu mmojhi mawu la ekima, ni mwina mawu lojhiwa umowakondela Mzimu mmeneyo. Mzimu umweo umpacha mwina kukhoza kukhulupilila kwa kukulu, ni mwina wampacha kukhoza kulamicha odwala. Mzimu umpacha mwina mbhaso yochita vodabwicha, mwina wampacha ulosi, mwina wampacha kusiyanicha mbhaso zichoka kwa Mnungu ni opande kwa Mnungu, mwina wampacha kukamba mikambo ya chilendo, mwina mbhaso yotambulila mikambo ya chilendo. Ivi vonjhe yachitika ni Mzimu mmojhi, ni mzimu umenewo nde uwo umpacha kila mundhu mbhaso yake.

Nifuna mujhiwe kuti mundhu waliyonjhe uyo wachogozedwa ni Mzimu wa Mnungu, siwakhoza kukamba, "Yesu walesedwe!" Chinchijha mundhu waliyonjhe siwakhoza kukamba "Yesu ni Ambuye," popande kuchogozedwa ni Mzimu wa Mnungu.

Simujhiwa kuti mathupi yanu ni nyumba ya Mzimu Wamnungu, uwo ukhala mkati mwanu ni uwo mwapachidwa ni Mnungu? Mathupi yanu osati yanu mwachinawene nambho ni ya Mnungu, pakuti mdaghulidwa kwa mtengo wa ukulu. Tumilani matupi yanu kwa ulemelelo wa Mnungu.

Zene mjhiwa kuti anyimwe ni nyumba ya Mnungu ni kuti Mzimu wa Mnungu ukhala mkati mwanu?

Palibe mundhu uyo wajhiwa maganizo ya mundhu mwina. Chimchijha mzimu wokha ulimkati nde ujhiwa maganizo ya mundhu mmeneyo, chimwecho ndeumo ili ata kwa Mnungu, Mzimu wokha wa Mnungu nde ujhiwa maganizo ya Mnungu.

Fruto do Espírito

O fruto do Espírito é amor, alegria, paz, paciência, bondade, fidelidade, mansidão e domínio próprio.

Nambho ivo vichokela ukachogozedwa ni Mzimu wa Mnungu ni chikondi, kukondwela, mtendele, kulimba mtima, ubwino, kutangatila wina ni kukhulupilika, wojhichicha ni kujhilamula umwene. Palibe thauko ilo lichogoza kuvichucha vindhu vimenevo.

Nambho ivo vichokela ukachogozedwa ni Mzimu wa Mnungu ni chikondi, kukondwela, mtendele, kulimba mtima, ubwino, kutangatila wina ni kukhulupilika,

Chikhulupi chimenecho sichitiphecha mtima, ndande Mnungu wathothila chikondi chake mmitima mwathu kwa njila ya mzimu woyela iyo wadatipacha.

Pakuti ufumu wa Mnungu osati kudya ni kumwa, nambho ni kukahala ukhalo uwo umkhwadilicha Mnungu, mtendele ni kukondwela uko kupelekedwa ni mzimu wa Mnuungu.

Mnungu wa chikhulupi uyo wakuthilani anyiimwe mtima ni mtendele pa kumkhulupilila, mpate kujhazidwa ni chikhululupilo chachikulu kwa mbhavu za mzimu wa Mnungu.

Não entristeçais o Espírito

Não entristeçais o Espírito Santo de Deus. Não apaguem o Espírito — antes, enchei-vos dele continuamente.

Simudamdandaulicha Mzimu wa Mnungu, pakuti Mzimu umeneo ni chizindikilo cha Mnungu kwanu kuti anyiimwe ni wandhu wake, ni uchimikizo ndande ya siku la uomboli.

Simudamdandaulicha Mzimu wa Mnungu, pakuti Mzimu umeneo ni chizindikilo cha Mnungu kwanu kuti anyiimwe ni wandhu wake, ni uchimikizo ndande ya siku la uomboli.

Msiye kulojhela mowa, imeneyo siikutaizeni, nambho mchoghozedwe ni Mzimu wa Mnungu.

nde uyo wadatiika chizindikilo chilangiza kuti ife niwandhu wake ni kutipacha Mzimu mmitima mwathu, kutichimikizila kuti siwatipache vindhu vonjhe ivo watiikila.

Yapa "Ambuye" nde Mzimu, ni yapo wali Mzimu wa Ambuye nde yapo pali ufulu.

Yapa "Ambuye" nde Mzimu, ni yapo wali Mzimu wa Ambuye nde yapo pali ufulu.

O Espírito nos capacita

O Espírito intercede por nós, batiza e capacita para o serviço. Ele é poder para a missão e conforto na aflição.

Yusufu yapo wamaganizila chindhu ichi, Mtumiki wa kumwamba wa Ambuye wadamjhela kumaloto kumkambila Yusufu mwana wa Daudi, Usadaopa kumtenga Maliya kukhala mkazako pakuti pathupi pake pajha kwa mbhavu za Mzimu Woyela.

Yapo sakupelekeni kubwalo la milandu, msadakhala ni mandha kuti simukambe chiyani, pakuti simupachidwe chokamba ndhawi imeneyo. Pakuti osati anyiimwe mukamba, nambho Mzimu Woyela wa Mnungu siukambe kupitila anyiimwe."

"Zene nikukambilani, awili pakati panu akavomelezana pajhiko la panjhi kuusu chilichonjhe icho afuna kupembha, Atate wanga a kumwamba siakuchitileni. Pakuti yapo asonghana wandhu awili kapina atatu kwa jhina langa, ine nili pamojhi nao."

Chipano pitani kwa wandhu maiko yonjhe, mkaachite kukhala oyaluzidwa, mkaabatize kwa jhina la Atate ni la Mwana ni la Mzimu Woyela, ni mwaayaluze kuyagwila yonjhe yayo nakulamulilani. Zenedi, ine nili pamojhi namwe muyaya mbaka mathelo ya jhiko la panjhi."

Yapo siakugwileni ni kukupelekani ku bwalo la milandu, msadaganizila chokamba. Ndhawi ikajha kambani chalinjhonjhe icho simpachidwe, pakuti osati anyiimwe simkambe nambho Mzimu Woyela.

Kubatizidwa kwa Yesu

Yapo wandhu wonjhe adali kubatizidwa, Yesu nayonjho wadabatizidwa. Ni yapo wadali kupembhela, kumwamba kudachekuka. Ndiipo Mzimu Woyela uwo umaoneka ngati nghunda udamchikila. Ni mvekelo kuchokela kumwamba udaveka, "Iwe nde mwana wanga uyo nikukonda, nakondelechedwa ni iwe."

"Mzimu wa Ambuye uli mkati mwanga,

pakuti wanisangha

kwaakambila wosauka uthenga wabwino.

Anituma kuti nauzile wandhu womangidwa ufulu wao,

ni wosapenya akhoze kuonanjho,

ni kwaapacha ufulu yawo aoneledwa.

"Mzimu wa Ambuye uli mkati mwanga,

pakuti wanisangha

kwaakambila wosauka uthenga wabwino.

Anituma kuti nauzile wandhu womangidwa ufulu wao,

ni wosapenya akhoze kuonanjho,

ni kwaapacha ufulu yawo aoneledwa.

Ni kuuzila chaka cha Ambuye icho chavomelezedwa."

Chipano ngati anyiimwe, yawo muli wolakwa, mujhiwa kwapacha wana wanu vindhu vabwino, zenedi Atate wanu wakumwamba sayendekele kupunda kwapacha Mzimu Woyela yawo ampembha."

Seja o primeiro