Nem só de pão vive o homem
'Nem só de pão vive o homem' — essa declaração de Jesus ao diabo no deserto revela que a Palavra de Deus é o verdadeiro alimento que sustenta a vida em plenitude.
O verdadeiro alimento
Quando tentado a transformar pedras em pão, Jesus respondeu com a Escritura: a vida humana depende de toda palavra que sai da boca de Deus.
Yesu wadamuyangha, "Yalembedwa, ‘Mundhu siwakhala wa moyo kwa bumundape, Nambho kwa kila malembo yoyela yakambidwa ni Mnungu.’"
Ndiipo Satana wadamkambila, "Ngati iwe ni mwana wa Mnungu, ng’anamula mwala uu ukhale bumunda." Yesu wadamuyangha, "Yalembedwa mumalembo ya Mnungu, ‘Mundhu siwangakhale ni umoyo kwa kudya bumundape.’ "
Jesus, o pão vivo
Jesus é o pão da vida que desceu do céu. Quem come deste pão viverá para sempre. Ele é o sustento que satisfaz a fome da alma.
Chimwecho wadaakambila, "Ine nde chakudya cha umoyo. Uyo wakujha kwanga siwaona njala ni uyo wanikhulupilila siwaona lujho muyaya.
Ine nde chakudya cha umoyo.
Ine nde chakudya chili cha moyo icho chachika kuchoka kumwamba. Mundhu waliyonjhe uyo siwadye chakudya ichi siwakhale moyo muyaya. Ni chakudya icho sinimpache, nde thupi langa ilo nichocha ndande ya wandhu ajhiko la panjhi."
Ngati umo Atate yawo ali amoyo adanitumila, nane nili wamoyo kupitila iwo, chimwecho uyo waniidya ine siwakhale moyo kupitila ine. Chino nde chakudya icho chachika kuchoka kumwamba, osati ngati mana iyo adadya azee wanu, ndiipo adamwalila. Uyo wakudya bumunda lino siwakhale moyo muyaya."
Buscar o Reino acima de tudo
Não andeis ansiosos pelo que comer ou beber. Buscai primeiro o Reino de Deus, e todas estas coisas vos serão acrescentadas.
"Ndendande nikukambilani msadajhichaucha pa umoyo wanu kuti simudye chiyani kapina simumwe chiyani kuti mkhale amoyo kapina mathupi yanu simuvale chiyani. Bwanji umoyo osati wa phindu kupitilila chakudya? Bwanji, thupi lilibe phindu kupitilila vivalo?
"Basi, msadajhisaucha mmitima yanu, kuti mukudya chiyani kapina mukumwa chiyani. Pakuti yameneyo yachauchilidwa kupunda ni wandhu wonjhe yawo samjiwa Mnungu. Nambho, Atate wanu a kumwamba ayajhiwa kuti muyafuna. Nambho, ufunefuneni uti ufumu wa Mnungu, ni vindhu ivi navo simupachidwe."
Ndhawi imweyo oyaluzidwa wake amampembelela Yesu, "Oyaluza, madyani ata pang’onope."
Ndiipo Yesu wadaakambila, "Ine nili ni chakudya icho simuchijhiwa."
Oyaluzidwa wake adamfunjha, "Bwanji, pali ni mundhu uyo wampelekela chakudya?"
Yesu wadayangha, "Chakudya changa nde ichi, kuchita icho wafuna uyo wanituma ni kuimaliza njhito yake.