24Pakuti kwa kukhulupila kumeko ife taomboledwa. Nambho kukhulupilila kulibe mate ngati tichiona chijha tichikhulupilila. Pakuti yani wakhulupilila chijha wachiona?
25Ngati tichikhulupila icho tilibe, chimwecho sitichilindile kwa kuchilimbila mtima.
35Niyani wakhoza kutiika patali nichikondi cha Kilisito? Bwanji ni kulaga, kapina mavuto, kapina njala, kapina kutedwa njhalu, kapina kuofyedwa kuphedwa?