Pular para o conteúdo
Publicidade

Afilipi 1:12-14

NTNYBL2025 Nyanja

Muomboli ndewatipacha umoyo

12 Okhulupila achanjanga, nifuna mujhiwe kuti vindhu vonjhe vanipata uzene vanitangatila kulalikila Uthenga Wabwino. 13 Kuchokana ni yamenyo, alonda onjhe anyumba ya Ufumu pamojhi ni wina, ajhiwa nalimndende ndande nimtumikila Kilisito. 14 Ndande ya kumangidwa kwanga kwa achita Okhulupilila ambili akhale ni chikhulupi kwa Ambuye, ata apata mbhavu yolalikila uthenga wa Mnungu popande mandha.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    12 Tsopano abale, ndikufuna mudziwe kuti chimene chandichitikira ine chathandiza kwambiri kupititsa patsogolo Uthenga Wabwino. 13 Chotsatira chake nʼchakuti zadziwika bwino lomwe kwa onse amene ali ku nyumba yaufumu kuti ine ndili mʼmaunyolo chifukwa cha Khristu. 14 Moti chifukwa cha maunyolo angawa, abale ambiri alimbikitsidwa kuyankhula Mawu a Mulungu molimbika ndi mopanda mantha.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Filipenses
Ver todos os capítulos de Filipenses