4Koma wansembe asadzidetse chifukwa cha anthu amene ali nawo pa ubale obwera chifukwa cha ukwati.
13" ‘Iye akwatire namwali wosadziwa mwamuna.
19munthu wa phazi lolumala kapena dzanja lolumala,
24 resultados encontrados
4Koma wansembe asadzidetse chifukwa cha anthu amene ali nawo pa ubale obwera chifukwa cha ukwati.
13" ‘Iye akwatire namwali wosadziwa mwamuna.
19munthu wa phazi lolumala kapena dzanja lolumala,
4Dziko lina la Akanaani ndi Ameara limene lili mʼmanja mwa Asidoni mpaka ku Afeki, dziko limene linachitana malire ndi dziko la Aamori.
2Israeli anene kuti:"Chikondi chake ndi chosatha."
3Banja la Aaroni linene kuti,"Chikondi chake ndi chosatha."
4Iwo amene amaopa Yehova anene kuti:"Chikondi chake ndi chosatha."
6Ndinamutsekulira wachikondi wanga,koma nʼkuti wachikondi wangayo atachoka; iye anali atapita.Mtima wanga unafumuka chifukwa cha kuchoka kwake.Ndinamuyangʼanayangʼana koma sindinamupeze.Ndinamuyitana koma sanandiyankhe.
8Inu akazi a ku Yerusalemu ndithu ndikukupemphani,mukapeza wokondedwa wangayo,kodi mudzamuwuza chiyani?Muwuzeni kuti ine ndadwala nacho chikondi.Abwenzi
10Wokondedwa wangayo ndi wowala kwambiri ndi wathanzipakati pa anthu 1,000.