Publicidade

Anjos

Por Bíblia Online

Os anjos são seres celestiais criados por Deus para servir, adorar e executar seus propósitos. A Bíblia revela anjos mensageiros, guerreiros e protetores ao longo de toda a história redentora.

Yusufu yapo wamaganizila chindhu ichi, Mtumiki wa kumwamba wa Ambuye wadamjhela kumaloto kumkambila Yusufu mwana wa Daudi, Usadaopa kumtenga Maliya kukhala mkazako pakuti pathupi pake pajha kwa mbhavu za Mzimu Woyela.

Mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadaakambila wachikazi wajha, "Msadaopa! Nijhiwa kuti mumfunafuna Yesu uyo wadapachikidwa pamtanda. Palibemo muno, wathohyuka ngati mujha iye wadakambila. Majhani mpenye malo yayo adamuika.

Bwanji, simjhiwa kuti nikhoza kwatana Atate wanga anithangatile, ni iwo akhoza kunipelekela magulu khumi ni yawili ya atumiki akumwamba?

Nambho mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadamkambila, "Maliya usadaopa, pakuti Mnungu wakupacha mwawi. Vechela, siupate pathupi ni kubala mwana wa mmuna, niiwe siumpache jhina Yesu.

Nambho mtumiki wa kumwamba wa Mnungu wadaakambila, "Msadaopa! Nakupelekelani uthenga wabwino uwo siwakondweleche kupunda wandhu wonjhe.

"Ulemelelo ukhale kwa Mnungu wali kumwamba kupunda

ni pano pajhiko lapanjhi pakhale ni mtendele

kwa wandhu yawo waakonda!"

Nikukambilani chimwecho, kuli chikondwelo pachogolo pa atumiki akumwamba a Mnungu ndande ya mundhu wochimwa mmojhi uyo walapa."

Maso yawo yapo yadali yakali kumpenyechecha kumwamba Yesu yapo wamapita, mwachizulumukila wachimuna awili yawo adavala njhalu zoyela adaima pambhepete pawo, adakamba, "Anyiimwe wandhu a ku Galilaya, ndande yanji muima pamenepo uku nimpenya kumwamba? Yesu uyo watengedwa kupita kumwamba, siwajhenjho ngati mujha mwamuwonela niwapita kumwamba."

Ata ngati, nikamba kwa mikambo ya wandhu ni atumiki akumwamba a Mnungu, nambho ngati nilibe chikondi, nikhala ngati mvekelo wa chibekete ichochilibe kandhu kapina chingwangwa.

Pakuti nijhiwa uzene kuti palibe chindhu chikhoza kutipatula ni chikondi cha Mnungu ikhakhala nyifa kapina umoyo, kapina atumiki a akumwamba kapina mbhavu zina za kumwamba, kapina yayo yachokela saino, kapina yayo siyachokele pambuyo, kapina ulamulilo, kapina jhiko la kumwamba kapina jhiko la panjhi kupunda. Palibe choumbidwa chalichonjhe chikhoza kutiika patali ni chikondi cha Mnungu mkati mwa Kilisito Yesu mbuye wathu.

Publicidade
Bíblia Online Bíblia Online

Bíblia Online • Versão: 2026-06-20_17-16-08-