Pular para o conteúdo
Publicidade

Batismo

Por Bíblia Online

O batismo é mandamento de Jesus e proclamação pública de fé. É símbolo de morte para o pecado, sepultamento com Cristo e ressurreição para uma vida nova no Espírito.

O mandamento de Jesus

Ide e fazei discípulos, batizando-os em nome do Pai, do Filho e do Espírito Santo. O batismo é porta de entrada na comunidade cristã.

Chipano pitani kwa wandhu maiko yonjhe, mkaachite kukhala oyaluzidwa, mkaabatize kwa jhina la Atate ni la Mwana ni la Mzimu Woyela, ni mwaayaluze kuyagwila yonjhe yayo nakulamulilani. Zenedi, ine nili pamojhi namwe muyaya mbaka mathelo ya jhiko la panjhi."

Yesu wadajha pafupi pao ni kwaakambila, "Napachidwa ulamulilo wa kuchogoza kumwamba ni jhiko lapanjhi. Chipano pitani kwa wandhu maiko yonjhe, mkaachite kukhala oyaluzidwa, mkaabatize kwa jhina la Atate ni la Mwana ni la Mzimu Woyela, ni mwaayaluze kuyagwila yonjhe yayo nakulamulilani. Zenedi, ine nili pamojhi namwe muyaya mbaka mathelo ya jhiko la panjhi."

Yesu wabatizidwa

Ndhawi imeneyo Yesu wadachoka ku Galilaya ni kufika ku mchinje Yolodani kuti Yohana wambatize.

Mundhu waliyonjhe uyo wakhulupilila ni kubatizidwa, siwaomboledwe, nambho mundhu uyo wakana kukhulupilila siwalamulidwe.

Chimwecho wadaakambila, "Pitani kujhiko lonjhe la panjhi, mkalalikile wandhu wonjhe Uthenga Wabwino. Mundhu waliyonjhe uyo wakhulupilila ni kubatizidwa, siwaomboledwe, nambho mundhu uyo wakana kukhulupilila siwalamulidwe.

Yesu wabatizidwa ni kuyesedwa

Ndhawi imeneyo Yesu wadachokela mmujhi wa Nazaleti, mujhiko la Galilaya, wadafika kwa Yohana, nayo wadambatiza mumchinje Yolodani. Yesu yapo wadachuuka mmajhi, pamwepo wadaona kumwamba kwamasulidwa, ni Mzimu Woyela udamchikila ngati nghunda.

Morrer e ressuscitar

Fomos sepultados com Cristo pelo batismo na morte para que andemos em novidade de vida. O batismo é renascimento pelo Espírito.

Mjhiwa ife tidabatizidwa tidalunjana ni Yesu Kilisito, tidabatizidwa ni kulunjana ni nyifa yake. Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.

Mjhiwa ife tidabatizidwa tidalunjana ni Yesu Kilisito, tidabatizidwa ni kulunjana ni nyifa yake.

Notho! Ife tayafela machimo, sitiendekele bwanji kukhala mmachimo? Mjhiwa ife tidabatizidwa tidalunjana ni Yesu Kilisito, tidabatizidwa ni kulunjana ni nyifa yake. Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.

Pakuti ife talunjana niiye kwa njila nyifa yake, chimwecho ife sitilunjane naye kwa kuhyukichidwa ngati iye. Tijhiwa kuti vichito vathu va kale vidafa ni vidapachikidwa pa mtanda pamojhi niiye, kuti mbhavu za machimo ziwanangidwe, ni sitidakhalanjho akapolo a machimo. Mundhu wakafa kwa mtundu umeneo siwakhaliletu hulu kuchokela mmbhavu za machimo.

Kwa njila ya kumkhulupilila Yesu anyiimwe mwaonjhe mwakala wana Amnungu kwa kulunjhana ni Kilisito Yesu. Anyiimwe onjhe mwabatizidwa ni kulunjana ni Kilisito, chipano mwalingana ni Kilisito.

Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu

Yesu wadayangha, "Uzene nikukambila, mundhu ngati siwabadwa kwa majhi ni Mzimu, siwakhoza kulowa mu Ufumu wa Amnungu

Batismo e Espírito

Arrependei-vos e cada um seja batizado. O batismo no Espírito Santo é poder para vida e testemunho.

Petulo wadaayangha, "Lapani, kila mmojhi wanu mmbatizidwe kwa jhila la Yesu Kilisito, kuti mlekeleledwe machimo yanu ni kulandila ahadi ijha ya Mzimu Woyela.

Petulo wadaayangha, "Lapani, kila mmojhi wanu mmbatizidwe kwa jhila la Yesu Kilisito, kuti mlekeleledwe machimo yanu ni kulandila ahadi ijha ya Mzimu Woyela.

Wandhu ambili adakhulupilila mawu ya Petulo ni adabatizidwa, wandhu ngati elufu zitatu adawonjezekela pa gulu lawo siku limenelo.

Nambho Filipo wadalalilkila Uthenga Wabwino wa Ufumu wa Mnungu ni jhina la Yesu Kilisito, wandhu wonjhe adakhulupilila ni adabatizidwa, waachimuna kwa waachikazi. Simoni nayo wadakhulupilila Uthenga Wabwino ni kubatizidwa. Wadamchata Filipo kila kumalo, niwadabwa vizindikilo ni vodabwicha ivo wadaviona.

Yapo amayendekela ni ulendo adafika malo yayo yadali ni majhi, yujha wamkulu wadakamba, "Pano pali majhi. Chindhu chanji icho sichinichekeleze nisidabatizidwa?" Filipo wadamuyangha, "Ngati siumkhulupilile Yesu kwa mtima wako wonjhe, siubatizidwe." Yujha mundhu wadayangha, "Nikhulupilila kuti Yesu Kilisito ni Mwana wa Mnungu."

Wamkulu wadalamula kuti ngolo ijha iyimichidwe. Adachika, adabila mmajhi wonjhe awili, ni Filipo wadambatiza yujha wamkulu. Yapo adachuuka mmajhi, Mzimu wa Ambuye udamnyakula Filipo, nayo wamkulu yujha siwadamuonenjho, nambho wadayendekela ni ulendo wake uku niwakondwa.

"Wandhu anyiyawa alandila Mzimu Woyela, ngati umo tidamlandilila ife. Bwanji, pali mundhu waliyonjhe uyo wakhoza kukaniza kuti saadabatizidwa kwa majhi?" Chimwecho wadalamula kuti abatizidwe kwa jhina la Yesu Kilisito. Basi wandhu anyiwajha adampembha Petulo wakhale ni anyiiwo kwa masiku yochepa.

"Wandhu anyiyawa alandila Mzimu Woyela, ngati umo tidamlandilila ife. Bwanji, pali mundhu waliyonjhe uyo wakhoza kukaniza kuti saadabatizidwa kwa majhi?"

Poolo wadakamba, "Ubatizi uwo wamayaluza Yohana udali wa kulapa, wadaakambila wandhu amkhulupilile iye uyo wakujha pambuye pake, yaani Yesu."

Ochatila achameneo yapo adavela chimwecho, adabatizidwa mujhina la Ambuye Yesu. Poolo wadaasanjika manja, ni Mzimu Woyela adachikila anyiiwo, ni kuyamba kukamba mikambo yachilendo ni adayamba kuuzila Uthenga wa Mnungu.

Ochatila achameneo yapo adavela chimwecho, adabatizidwa mujhina la Ambuye Yesu.

Poolo wadaasanjika manja, ni Mzimu Woyela adachikila anyiiwo, ni kuyamba kukamba mikambo yachilendo ni adayamba kuuzila Uthenga wa Mnungu.

Chipano siufunika kulindila ndhawi yaitali. Ima ubatizidwe ni kuelechedwa machimo yako dala ulekeleledwe kwa kukhulupilila jhina la Ambuye."

Yohana wadaabatiza wandhu kwa majhi, nambho posachedwa simubatizidwe kwa Mzimu Woyela."

Nambho simujhazidwe mbhavu yapo siwajhe kwanu Mzimu woyela, ni anyiimwe simukhale amboni wanga mmijhi ya Yelusalemu, Yudea yonjhe ni Samaliya, ni jhiko lonjhe lapanjhi."

Yapo adangomaliza kupembhela, pamalo pajha adakomanilana padatingizika. Wandhu onjhe adajhazidwa ni Mzimu Woyela ni kukamba mau la Mnungu popande mandha.

Kubatizidwa kwa Yesu

Yapo wandhu wonjhe adali kubatizidwa, Yesu nayonjho wadabatizidwa. Ni yapo wadali kupembhela, kumwamba kudachekuka. Ndiipo Mzimu Woyela uwo umaoneka ngati nghunda udamchikila. Ni mvekelo kuchokela kumwamba udaveka, "Iwe nde mwana wanga uyo nikukonda, nakondelechedwa ni iwe."

Chipano ngati anyiimwe, yawo muli wolakwa, mujhiwa kwapacha wana wanu vindhu vabwino, zenedi Atate wanu wakumwamba sayendekele kupunda kwapacha Mzimu Woyela yawo ampembha."

Um batismo

Em um Espírito fomos todos batizados em um só corpo. O batismo é um só, assim como um só é o Senhor e uma só é a fé.

Pakuti kwa Mzimu mmojhi, taonjhe tidabatizidwa kwa thupi limojhi, atangati Ayahudi kapina Agiliki, akapolo au osati akapolo, ni taonjhe tapachidwa ni Mzimu mmojhi.

Pakuti kwa Mzimu mmojhi, taonjhe tidabatizidwa kwa thupi limojhi, atangati Ayahudi kapina Agiliki, akapolo au osati akapolo, ni taonjhe tapachidwa ni Mzimu mmojhi.

Bwanji, Kilisito wadajhipatula magulumagulu? Bwanji, Poolo nde uyo wadapachikidwa pa mtanda ndande yanu? Bwanji mudabatizidwa ngati oyaluzidwa a Poolo?

Naayamika Amnungu pakuti sinidambatize waliyonjhe pakati panu, nambho Kilisipo ni Gayo pe. Chimwecho palibe uyo wakhoza kukambi wabatizidwa kuti wakhale oyaluzidwa wanga. Nakumbukila, nidambatiza Sitefano ni wandhu amnyumba mwake, nambho sinikumbukila ngati nidambatiza mundhu mwina waliyonjhe. Kilisito siwadanitume kubatiza. Wanituma kulalikila Uthenga Wabwino, nilalikile popande kukhulupilila mawu ya hekima za wandhu, dala mbhavu ya nyifa ya Kilisito pamtanda siidaoneka yopandemate.

Ine sinimamjhiwe, nambho uyo wanituma kubatiza wandhu kwa majhi wanikambila, Mundhu uyo siwauone mzimu niuchika kuchoka kumwamba ni kukhala pa mwamba pake, nde uyo wabatiza kwa Mzimu Woyela.

Ine sinimamjhiwe, nambho uyo wanituma kubatiza wandhu kwa majhi wanikambila, Mundhu uyo siwauone mzimu niuchika kuchoka kumwamba ni kukhala pa mwamba pake, nde uyo wabatiza kwa Mzimu Woyela.

Seja o primeiro