Pular para o conteúdo
Publicidade

Casamento

Por Bíblia Online

O casamento é aliança sagrada instituída por Deus. Ele une marido e mulher em uma só carne — pacto de amor, fidelidade e companheirismo que reflete o amor de Cristo pela Igreja.

Fundamento divino

Não é bom que o homem esteja só. Deus criou o casamento como aliança de companheirismo, amor e fecundidade.

Fidelidade conjugal

O que Deus ajuntou não separe o homem. O casamento deve ser honrado e o leito matrimonial preservado sem impureza.

Chimwecho, anyiiwo osati awilinjho, nambho thupi limojhi. Icho wachilunjanicha Mnungu, mundhu siwadachisiyanicha."

Yesu wadaayangha, wadakamba, "Bwanji, simudasome Mmalembo Yoyela kuti poyamba Mnungu wadamuumba mundhu wammuna ni wamkazi? Mnungu wadakamba, Pandande iyi mundhu wammuna siwaasiye atate wake ni maye wake ni kulunjana ni mkazake, ni awili yawa siakhale thupi limojhi.Chimwecho, anyiiwo osati awilinjho, nambho thupi limojhi. Icho wachilunjanicha Mnungu, mundhu siwadachisiyanicha."

Mnungu wadakamba, Pandande iyi mundhu wammuna siwaasiye atate wake ni maye wake ni kulunjana ni mkazake, ni awili yawa siakhale thupi limojhi.Chimwecho, anyiiwo osati awilinjho, nambho thupi limojhi. Icho wachilunjanicha Mnungu, mundhu siwadachisiyanicha."

Nghani za talaka

"Idathokambidwanjho, Mundhu waliyonjhe wakafuna kumleka mkazake ifunika wampache talaka.Nambho ine nikukambilani mundhu waliyonjhe uyo siwamsiye mkazake kwa ndande yaliyonjhe ijha ni osati kwa ndande ya chigololo wamchita mkazake kukhala wachigololo, ni wammuna waliyonjhe uyo siwamkwate wamkazi uyo wasiidwa nayo wachita chigololo."

Mayaluzo kuusu chigololo

Yesu wadaendekela kukamba, "Mwavela kuti wandhu adakambilidwa, Usadachita chigololo!Nambho ine nikukambilani kuti uyo siwampenye wamkazi kwa kumkhumbila wathochita chigololo mumtima mwake.

Anyiiwo adamuyahga, "Musa wadaagiza wammuna wakhoza kulemba talaka ni kumsiya wamkazi."

Yesu wadaakambila, "Musa wadakulembelani lamulo limenelo ndande simuyaluzika. Nambho, kuyambila kuumbidwa kwa jhiko, Mnungu wadaumba wamuna ni wamkazi. Chimwecho, wamuna siwasiye atate wake ni amake ni kulunjana ni mkazake, ni anyiiwo awili sakhale thupi limojhi. Chipano anyiiwo osati awilinjho, nambho ni thupi limojhi. Chimwecho, icho wachilunjanicha Mnungu, mundhu siwadachisiyanicha."

Chinchijha, wamkazi wakamsiya mmunake ni kupita kukwatiwa ni wammuna mwina, wamchitila chigololo mmunake."

Amor como Cristo

Maridos, amai vossas mulheres como Cristo amou a igreja. O amor conjugal reflete o evangelho em ação.

Anyiimwe wachimuna, mjhakonda achakazanu ngati Kilisito umo wadalikondela gulu lake, wadajhichocha njhembe ndande yawo, dala kwa mawu lake, walipatule kwa Mnungu kwa kulichuka mumajhi,

Anyiimwe wachimuna, mjhakonda achakazanu ngati Kilisito umo wadalikondela gulu lake, wadajhichocha njhembe ndande yawo, dala kwa mawu lake, walipatule kwa Mnungu kwa kulichuka mumajhi, dala wapate gulu la wandhu amkhulupilila, ilo la sanghidwa ndande ya Mnungu ni labwino, gulu ilo lilibe machimo, kupunduka kapina chilichonjhe cha mtundu umeneo.

Anyiimwe wachimuna, mjhakonda achakazanu ngati Kilisito umo wadalikondela gulu lake, wadajhichocha njhembe ndande yawo, dala kwa mawu lake, walipatule kwa Mnungu kwa kulichuka mumajhi, dala wapate gulu la wandhu amkhulupilila, ilo la sanghidwa ndande ya Mnungu ni labwino, gulu ilo lilibe machimo, kupunduka kapina chilichonjhe cha mtundu umeneo. Chimwecho wachimuna afunika kwakonda achakazao ngati matupi yawo. Uyo wamkonda mkazake mmeneyo wajhikonda mwene. Palibe mundhu uyo waliipila thupi lake, nambho walidyecha ni kuliveka. Nde umo Kilisito walisungila gulu lake, pakuti ife ni viwalo va thupi lake.

Chimwecho wachimuna afunika kwakonda achakazao ngati matupi yawo. Uyo wamkonda mkazake mmeneyo wajhikonda mwene.

Chimwecho wachimuna afunika kwakonda achakazao ngati matupi yawo. Uyo wamkonda mkazake mmeneyo wajhikonda mwene. Palibe mundhu uyo waliipila thupi lake, nambho walidyecha ni kuliveka. Nde umo Kilisito walisungila gulu lake, pakuti ife ni viwalo va thupi lake.

Anyiimwe wachikazi mjhavela achamunanu ngati kwa vela Ambuye Yesu. Mate yake wammuna nayo wali ni ulamuli kwa mkazake, ngati umo Kilisito wali ni ulamuli kwa gulu la wandhu amkulupilila Kilisito, ndande Kilisito mwene wake nde waliombola gulu limenelo ni nde thupi lake. Ngati umo gulu la wandhu amkhulupilila Kilisito limvelela iye, chimchijha wachikazi ajhavela achamunao kwa vindhu vonjhe.

Anyiimwe wachikazi mjhavela achamunanu ngati kwa vela Ambuye Yesu. Mate yake wammuna nayo wali ni ulamuli kwa mkazake, ngati umo Kilisito wali ni ulamuli kwa gulu la wandhu amkulupilila Kilisito, ndande Kilisito mwene wake nde waliombola gulu limenelo ni nde thupi lake.

Anyiimwe wachikazi mjhavela achamunanu ngati kwa vela Ambuye Yesu. Mate yake wammuna nayo wali ni ulamuli kwa mkazake, ngati umo Kilisito wali ni ulamuli kwa gulu la wandhu amkulupilila Kilisito, ndande Kilisito mwene wake nde waliombola gulu limenelo ni nde thupi lake. Ngati umo gulu la wandhu amkhulupilila Kilisito limvelela iye, chimchijha wachikazi ajhavela achamunao kwa vindhu vonjhe.

Anyiimwe wachimuna, mjhakonda achakazanu ngati Kilisito umo wadalikondela gulu lake, wadajhichocha njhembe ndande yawo, dala kwa mawu lake, walipatule kwa Mnungu kwa kulichuka mumajhi, dala wapate gulu la wandhu amkhulupilila, ilo la sanghidwa ndande ya Mnungu ni labwino, gulu ilo lilibe machimo, kupunduka kapina chilichonjhe cha mtundu umeneo. Chimwecho wachimuna afunika kwakonda achakazao ngati matupi yawo. Uyo wamkonda mkazake mmeneyo wajhikonda mwene. Palibe mundhu uyo waliipila thupi lake, nambho walidyecha ni kuliveka. Nde umo Kilisito walisungila gulu lake, pakuti ife ni viwalo va thupi lake. "Chimwecho, wammuna siwaasiye atate wake ni amaye wake, siwalunjane ni mkazake nao awili sakhale thupi limojhi." Kuli ni uzene uwo wabisika pa mawu yaya, ila ine nakamba nghani ya Kilisito ni gulu ilo la mkhulupilila. Nambho kila wammuna ifunika wamkonde mkazake ngati mwene wake ni wamkazi wafunika kumsamala mmunake.

"Chimwecho, wammuna siwaasiye atate wake ni amaye wake, siwalunjane ni mkazake nao awili sakhale thupi limojhi."

Nambho kila wammuna ifunika wamkonde mkazake ngati mwene wake ni wamkazi wafunika kumsamala mmunake.

Nambho kila wammuna ifunika wamkonde mkazake ngati mwene wake ni wamkazi wafunika kumsamala mmunake.

Anyiimwe ni wandhu a Mnungu, chimwecho chighololo, ukhalo waliyojhe woipa kapina chipili, sividakhala pakati panu, pakuti anyiimwe ni wandhu a Mnungu.

Submissão e respeito

Mulheres, sujeitem-se aos próprios maridos. Maridos, convivam com as esposas com conhecimento e honra.

Pureza no casamento

Não adulterarás. A impureza sexual destrói alianças e famílias. Deus chama à santidade no matrimônio.

Nambho chimo la chigololo ni loyipa, chimwecho kila wammuna wakhale ni wamkazi wake, ni kila wamkazi wakhale ni wammuna wake.

Wammuna wachite umo ifunikila kwa mkazake, ni wamkazi wachite umo ifunikila kwa mmunake, ni kila mmojhi wamkwaniliche mnjake icho chifunika. Wamkazi walibe lamulo pamwamba pa thupi lake, nambho mmunake wali nilamulo pamwamba pa thupi la mkazake, chinchijha wammuna nayonjho walibe lamulo pamwamba pathupi lake, nambho mkazake wali nilamulo pa mwamba pathupi la mmunake.

Wammuna wachite umo ifunikila kwa mkazake, ni wamkazi wachite umo ifunikila kwa mmunake, ni kila mmojhi wamkwaniliche mnjake icho chifunika. Wamkazi walibe lamulo pamwamba pa thupi lake, nambho mmunake wali nilamulo pamwamba pa thupi la mkazake, chinchijha wammuna nayonjho walibe lamulo pamwamba pathupi lake, nambho mkazake wali nilamulo pa mwamba pathupi la mmunake. Msadamanana nambho ikakhala mwavomelezana dala mpheze ndhawi ya mapembhelo, ndiipo mbwelelenjho ili Mdani wa Mnungu siwadapheza kukuikani mmayeso ndande ya kulepela kuchekeleza mafuno yanu.

Wammuna wachite umo ifunikila kwa mkazake, ni wamkazi wachite umo ifunikila kwa mmunake, ni kila mmojhi wamkwaniliche mnjake icho chifunika. Wamkazi walibe lamulo pamwamba pa thupi lake, nambho mmunake wali nilamulo pamwamba pa thupi la mkazake, chinchijha wammuna nayonjho walibe lamulo pamwamba pathupi lake, nambho mkazake wali nilamulo pa mwamba pathupi la mmunake. Msadamanana nambho ikakhala mwavomelezana dala mpheze ndhawi ya mapembhelo, ndiipo mbwelelenjho ili Mdani wa Mnungu siwadapheza kukuikani mmayeso ndande ya kulepela kuchekeleza mafuno yanu.

Chipano nikukambilani anyiimwe simuda kwate, nimwafedwa ni achamunanu, mbasa muendekele kukhala popande kukwata ni kukwatiwa ngati umo nili ine. Nambho ngati simukhoza kuchekeleza makhumbilo yanu, chimwecho mkwate kapina kukwatiwa, pakuti mbasa kukwata kapina kukwatiwa kusiyana nikuhla ni kukhumbila.

Nambho kwa anyiwajha akwata nili ni lamulo. Wamkazi siwadasiyana ni mmunake, nambho ikakhala wamkazi wasiyana nimmunake, siwada kwatiwa, kapina wabwelelane ni mmunake, ni wammuna siwadalemba kalata ya kumsiya mkazake.

Kwa wammuna siwadakhulupile walandilidwa kwa Mnungu kwa kulunjana ni mkazake, ni wamkazi siwada khulupilile walandilidwa ni Mnungu kwa kulunjana ni wammuna wamkhulupilila Kilisito. Ngati siidakali chimwecho wana wanu sadakavomelezedwa ni Mnungu, kumbe chipano avomelezedwa kukhala wana a Mnungu.

Nidakakonda anyiimwe msamakhaikila. Mundhu uyo walibe wamkazi wapota njhito ya Ambuye, ni ndande wafuna kumkondwelecha Ambuye. Nambho wammuna uyo wakwata wapota njhito pavindhu va jhiko dala wamkondweleche mkazake, ni waguzidwa kawili. Wammkazi siwada kwatiwe wajhi vuticha ni vindhu va Ambuye, nambho wammkazi wakwatiwa wajhichaucha ni vindhu va jhiko lino kuti wamkondweleche mmunake.

Wammkazi wakwatiwa wamangidwa ni thauko ngati pe wammuna wali wamoyo, nambho ngati wammuna wamwalila basi wamkazi mmeneyo wakakonda wakhoza kukwatiwa ni wammuna mwina, nambhope wakwatiwe ni wammuna uyo wamkhulupilila Yesu.

Mayaluzo ya nghani ya Ukwati

Chipano, kuchokana ni zijha nghani mdalemba.

Anyiimwe mdafunjha kuti ni mbasa wammuna siwadakwata. Nambho chimo la chigololo ni loyipa, chimwecho kila wammuna wakhale ni wamkazi wake, ni kila wamkazi wakhale ni wammuna wake.

Chithaweni chigololo. Machimo yina yonjhe wachita mundhu wachita kubwalo kwa thupi lake, nambho mundhu uyo wachita chigololo wachita mkhati mwathupi lake mwene wake. Simujhiwa kuti mathupi yanu ni nyumba ya Mzimu Wamnungu, uwo ukhala mkati mwanu ni uwo mwapachidwa ni Mnungu? Mathupi yanu osati yanu mwachinawene nambho ni ya Mnungu, pakuti mdaghulidwa kwa mtengo wa ukulu. Tumilani matupi yanu kwa ulemelelo wa Mnungu.

Ukhoza kukamba, "Chakudya ndande ya mimba, ni mimba ndande ya chakudya." Yetu, nambho Mnungu siwaviwanange vonjhe. Thupi osati ndande ya chigololo, nambho kwa kwaatumikila Ambuye, ni Ambuye ayasunga mathupi yathu ni kuyapacha chakudya. Mnungu wadahyukicha Ambuye Yesu, ni siwatihyukichenjho ife kwa mbhavu zake.

Zene mujhiwa kuti anyiyawo achita voipa siapata ufumu wa Mnungu. Simdanyengeka Achigololo, kapina alambila viboliboli kapina akomana chithupi kumbuyo kwa maumbidwe, kapina anghungu, kapina akhumbila kuipa, kapina alojhela, kapina otukwana, kapina alanda anyiyawa siaupata Ufumu wa Mnungu.

Uyo wali ni chikondi waembekeza, wathangatila, uyo wali nichikondi walibe njhanje, walibe dama, kapina kujhiona, uyo wali ni chikondi siwachepa ulemu, uyo wali ni chikondi siwafuna vindhu va kumthangatila mwene, kapina mbhwai za msanga, siwasunga chikumbukilo cha voipa, mundhu wa chikondi siwakondwela voipa, nambho chikondwela uzene. Mundhu wachikondi wapilila yonjhe, mundhu wa chikondi wakhulupila wina, mundhu wa chikondi waembekeza, ni siwalepela.

Bwanji, Kilisito wadajhipatula magulumagulu? Bwanji, Poolo nde uyo wadapachikidwa pa mtanda ndande yanu? Bwanji mudabatizidwa ngati oyaluzidwa a Poolo?

Naayamika Amnungu pakuti sinidambatize waliyonjhe pakati panu, nambho Kilisipo ni Gayo pe. Chimwecho palibe uyo wakhoza kukambi wabatizidwa kuti wakhale oyaluzidwa wanga. Nakumbukila, nidambatiza Sitefano ni wandhu amnyumba mwake, nambho sinikumbukila ngati nidambatiza mundhu mwina waliyonjhe. Kilisito siwadanitume kubatiza. Wanituma kulalikila Uthenga Wabwino, nilalikile popande kukhulupilila mawu ya hekima za wandhu, dala mbhavu ya nyifa ya Kilisito pamtanda siidaoneka yopandemate.

Chigololo chiwananga gulu lamkhulupilila Yesu

Navela kuti kwanu kuli chigololo, ni chigololo icho sichidakhalepo ata kwa wandhu yao siamjhiwa Mnungu, nakambilidwa pakati panu mmojhi wakhala ni wamkazi wa atate wake. Namwe mujhidama, bwanji ata simudandaula, nikumchocha pakati panu mmeneyo wachita chigololo chimenecho.

Sabedoria conjugal

Acha esposa, acha o bem. Bebe água da tua própria cisterna. A fidelidade conjugal é fonte de bênção permanente.

Bíblia e casamento

Deus abomina o divórcio. A aliança matrimonial é reflexo da aliança de Deus com seu povo — sagrada e eterna.

Poolo wakaniza wandhu kulunjana ni wandhu samkhulupilila Mnungu

Msada gwilizana ni wandhu osakhulupilile Mnungu. Bwanji ubwino ni kuipa vikoza kukhala pamojhi? Dangalila ni mdima vikhoza bwanji kukhala pamojhi?

Exemplos bíblicos

O Cântico dos Cânticos celebra o amor conjugal. A Bíblia honra o casamento em toda a sua beleza e profundidade.

Juízo e restauração

O Senhor é testemunha do pacto conjugal. Casamentos quebrados podem ser restaurados pelo poder e graça de Deus.

Kudali wamkazi mmojhi mlosi wamatanidwa Ana, mwana wamkazi wa Fanueli, wafuko la Asheli wadali mzee kupunda. Pa umwali wake wadakwatiwa ni kukhala ni mmunake kwa vyaka saba, ndiipo mmunake wadamwalila.

"Ngati mundhu siwakakulalike ku ukwati, usadakhala pa mpando wa ulemu, pakuti ikhozeka pali mundhu mwina wa ulemu kupitilila iwe, yawo waikilidwa mpando umeneo,

Waliyonjhe uyo wamsiya mkazake ni kukwata wamkazi mwina, wachita chogololo. Ni wammuna uyo wamkwata wamkazi uyo wasiyidwa ni mmunake, wachitanayo chigololo.

Pa masiku ya Nuhu, wandhu amadya ni kumwa, amakwata ni kukwatiwa mbaka siku lijha yapo Nuhu wadalowa mu chombo, kufulikila yapo mafuliko ya vula yayikulu yadachokela ni kuwapha wandhu ni vindhu vonjhe.

Yesu yapo wadaima wadamfunjha wamkaziyo, "Alikuti wajha wandhu akupacha mlandhu? Palibe waliyonjhe uyo wakulamula?"

Wamkazi mmeneyo wadayangha, "Wakulu, palibe waliyonjhe!"

Ndiipo Yesu wadamkambila, "Ata ine sinikulamula. Mapita siudachitanjho machimo."

Mundhu walionjhe uyo wasiya nyumba yake, kapina achakulu wake kapina mlongo wake kapina atate wake kapina maye wake kapina wana kapina munda ndande ya ine, mmeneyo siwachuluchidwe kambili kwa vijha walinavo ni siwaupate umoyo wamuyaya.

"Oyaluza, Musa wadakamba ngati mundhu wammuna wamwalila popande kusiya mwana, mbale wake wamkwate wamkazi wafedwa ni mmunake kuti wambalile mbalewake wana.

Wandhu yapo ahyuka palibe kukwata kapena kukwatiwa, siakhale ngati mtumiki wa kumwamba.

Pakuti mumtima yachoka maganizo ya kupha, chigololo, uhule, unami, kuba, umboni wanthila ni matukwano.

Vichito va jhiko vijhiwika navo nde ivi, uhule, chigololo, ni ukhalo woyipa, kulambila viboliboli, ufiti, udani, ndewo, njhanje, mbwayi, chipili, mkangano ni kosavana, kosakondwela mwina wakakhala ni chindhu, kulojhela mowa kudya kupunda ni vindhu vili ngati vimenevo. Nikuonyani ngati umo nidakuonyelani mmayambo, wandhu achita yameneyo saupata ufumu wa Amnungu.

Kwa chifani, wamkazi uyo wakwatiwa wamangidwa ni thauko ndhawi yonjhe yapo mmunake wakhala wamoyo, nambho mmunake wakamwalila, thauko limenelo silimmanganjho wamkazi mmeneyo. Chimwecho wamkazi mmeneyo wakakwatiwa ni wammuna mwina ndhawi iyo mmunake wali wamoyo, siwatanidwe wachighololo. Nambho mmunake wakamwalila, wamkazi mmeneyo siwamangidwanjho ni thauko la ukwati, ni wakakwatiwa ni wammuna mwina siwatanidwa wachighololo.

Seja o primeiro