Medo da morte
O medo da morte é universal, mas Cristo o venceu. A Bíblia ensina que para quem crê, a morte perdeu o aguilhão — não é mais motivo de terror, mas porta para a eternidade com Deus.
Cristo venceu a morte
Jesus assumiu carne e sangue para, pela morte, destruir o que tinha o poder da morte e libertar os que viviam em escravidão pelo medo dela.
Chimwecho thupi ili lakuwanangika yapo silivale kosawanangika, nalo thupi la kumwalila yapo sili vale kosamwalila, ndeyapo lijha mawu lalembedwa silikwanile "Nyifa yawanangidwa kwa kuikhoza!"
"Kuli pati kukhoza kwa nyifa?
Kuli pati kuwawa kwa nyifa?"
Nyifa, ipata mbhavu ya kupweteka kuchoka kumachimo, ni machimo yapata mbhavu ya kupweteka kuchoka mthauko. Nambho wayamikidwe Mnungu, iye watipacha kukhoza kwa kupitila Yesu Kilisito!
Yapo tidabatizidwa tidalunjana ni nyifa yake, tidazikidwa pamojhi niiye, kuti ngati mujha kilisito wadahyukichidwa kwa mbhavu yaikulu ya Atate, ife nafe tikhoze kukhala ni umoyo wa chipano.
Pakuti ife talunjana niiye kwa njila nyifa yake, chimwecho ife sitilunjane naye kwa kuhyukichidwa ngati iye.
A promessa da vida eterna
Quem ouve a Palavra e crê já passou da morte para a vida. O amor perfeito lança fora o medo, até o medo da morte.
"Zene nikukambilani, mundhu waliyonjhe uyo wavela mawu yanga ni kwaakhulupilila Amnungu yawo anituma, ali ni umoyo wa muyaya. Sialamulidwa muyaya, nambho wachoka kunyifa ni kulowa kuumoyo.
Yesu wadamkambila, "Ine nde uhyucho ni umoyo. Uyo wanikhulupilila ine atangati wakamwalila, siwakhale moyo,
Nikukambilani uzene, uyo wavela mawu yanga siwamwalila muyaya."
Mateyake Amnungu adaakonda wandhu a jhiko la panjhi ni kumchocha Mwana wao wa yokha, kuti kila uyo wamkhulupilila siwadatayika, nambho wakhale ni umoyo muyaya.
Não temas
Jesus disse: não temais os que matam o corpo. No vale da sombra da morte, o Senhor está conosco como pastor e protetor.
Msadaopa yawo akhoza kukuphani anyiimwe, nambho sakhoza kuyomwecha mizimu yanu. Nambho muopeni yujha wakhoza kuyomwecha thupi pamojhi ni mzimu mumoto wa muyaya.
Yalembedwa chimwechi mmalembo ya Mnungu, "Mundhu waliyonjhe uyo siwapembhe kwa ulamuli wa jhina la Ambuye siwaomboledwe."
Ngati umo malembo ya Mnungu yakambila,
"Ndande yako, tifunidwa ni nyifa usana ni usiku,
tawelengedwa ngati mbelele zopedwa."
Nambho pa vindhu vimenevo vonjhe, tikhoza ndande tithangatilidwa ni Klisito uyo watikonda. Pakuti nijhiwa uzene kuti palibe chindhu chikhoza kutipatula ni chikondi cha Mnungu ikhakhala nyifa kapina umoyo, kapina atumiki a akumwamba kapina mbhavu zina za kumwamba, kapina yayo yachokela saino, kapina yayo siyachokele pambuyo, kapina ulamulilo, kapina jhiko la kumwamba kapina jhiko la panjhi kupunda. Palibe choumbidwa chalichonjhe chikhoza kutiika patali ni chikondi cha Mnungu mkati mwa Kilisito Yesu mbuye wathu.