Pular para o conteúdo
Publicidade

Aefeso 4:17-19

NTNYBL2025 Nyanja

Umoyo wachipano ni umowo wakale

17 Chimwecho, nikuonyani kwa ulamulilo uwo napachidwa ni Ambuye. Msadakhalanjho ngati wandhu yao samjhiwa Mnungu, maganizo yao yali yoipa. 18 Njelu zao zili mumdima, alipatali ni umoyo wa Mnungu ndande ya usabobwa wao ni mitima yao yolimba. 19 Apanduka, alibe njhoni, ali ni ukhalo woyipa, ni apapalikila kupunda vindhu va manyazi va kila mtundu.

Em outras traduções

  1. TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo

    17 Tsono ine ndikukuwuzani izi, ndipo ndikunenetsa mwa Ambuye, kuti musayendenso monga amachitira anthu a mitundu ina potsata maganizo awo opanda pake. 18 Maganizo awo ndi odetsedwa, ndi osiyanitsidwa ndi moyo wa Mulungu chifukwa cha umbuli umene uli mwa iwo chifukwa cha kuwuma mtima kwawo. 19 Popeza sazindikiranso kanthu kalikonse, adzipereka okha kuti akhumbe zonyansa, kuti achite mtundu uliwonse wa zoyipa ndi zilakolako zosatha.

Direitos das traduções citadas

Estes versículos te tocaram? Ore agora!

+581 estão orando agora.

Junte-se à corrente de oração.

Efésios
Ver todos os capítulos de Efésios