8 Nambho ata ngati mmojhi wanu kapina mtumiki wa kumwamba wa Amnungu wakakulalikilani Uthenga wina uwo uoneneka ngati Uthenga Wabwino kusiyana ni ujha tidakulalikilani, walesedwe mundhu mmeneyo! 9 Ngati mujha tidakukambilani, ni saino nikambanjho, ngati mundhu waliyonjhe wakakulalikilani Uthenga wina kusiyana ni ujha mdalikidwa, walesedwe mundhu mmeneyo!
Publicidade
Agalatiya 1:8,9
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
8 Ngakhale ife kapena mngelo wochokera kumwamba, akalalikira Uthenga Wabwino wosiyana ndi umene tinakulalikirani uja, iyeyo akhale wotembereredwa! 9 Monga tanena kale, tsopano ndikubwereza kunenanso kuti, "Ngati wina aliyense akulalikirani Uthenga Wabwino wosiyana ndi umene munawulandira, iyeyo akhale wotembereredwa."
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.