6 Kumbukilani pa nghani za Ibulahimu, iye wadamkhulupilia Mnungu, ni kwa kukhulupilila kwake, Mnungu wadamvomela kuti iye ni wovomelezeka. 7 Chipano mjhiwe kuti wandhu yawo amkhulupilila Mnungu, achamenewo nde wana azene a Ibulahimu. 8 Malembo ya Mnungu yadatholangizilatu kuti Mnungu siwaachite wandhu kukhala wovomelezeka kwa kupitila khumkhulupilila Iye. Chimwecho malembo ya Mnungu yadachogholela kumkambila Ibulahimu Uthenga Wabwino uwo umakamba, "Kupitila iwe wandhu wonjhe sapachidwe mwawi." 9 Chipano, wajha akhulupilila apachidwa mwawi pamojhi ni Ibulahimu uyo wadakhulupilila.
Publicidade
Agalatiya 3:6-9
NTNYBL2025 Nyanja
Em outras traduções
- TCCL Abra a Palavra de Deus em Chichewa Contemporâneo
6 Nʼchimodzimodzinso Abrahamu, "Iye anakhulupirira Mulungu, ndipo Mulungu anamutenga kukhala wolungama."
7 Tsono zindikirani kuti amene akhulupirira, ndi ana a Abrahamu. 8 Malemba anaonetseratu kuti Mulungu adzalungamitsa anthu a mitundu ina mwachikhulupiriro, ndipo ananeneratu Uthenga Wabwino kwa Abrahamu kuti, "Mitundu yonse ya anthu idzadalitsika kudzera mwa iwe." 9 Choncho iwo amene ali ndi chikhulupiriro ndi odalitsidwa pamodzi ndi Abrahamu, munthu wachikhulupiriro.
Direitos das traduções citadas
Estes versículos te tocaram? Ore agora!
+581 estão orando agora.
Junte-se à corrente de oração.