Beleza
Por Bíblia Online
A verdadeira beleza vem de dentro. A Bíblia ensina que o encanto é enganoso e a formosura é vã, mas a mulher que teme ao Senhor — essa sim merece louvor.
Ife taumbidwa ni Mnungu kwa kulunjana ni Kilisito Yesu, dala tichite vichito vabwino ivo adatikonjekela tivichite kuyambila mmayambo.
Kukhala kwa chikhulupi
Chimwecho, sitikufa mtima ata ngati matupi yathu yalema ni kuzeeka, nambho mkati tichitidwa kukhala achipano kila siku.
"Ndendande nikukambilani msadajhichaucha pa umoyo wanu kuti simudye chiyani kapina simumwe chiyani kuti mkhale amoyo kapina mathupi yanu simuvale chiyani. Bwanji umoyo osati wa phindu kupitilila chakudya? Bwanji, thupi lilibe phindu kupitilila vivalo?
Seja o primeiro