Bíblia
A Bíblia é a Palavra de Deus — viva, eficaz e mais cortante que espada de dois gumes. Toda Escritura é inspirada por Deus e útil para ensinar, repreender, corrigir e instruir em justiça.
Inspiração divina
Toda Escritura é inspirada por Deus. Homens santos falaram da parte de Deus movidos pelo Espírito Santo.
Poder da Palavra
A Palavra de Deus é viva e eficaz. O céu e a terra passarão, mas as minhas palavras jamais passarão.
Kumwamba ni pajhiko sivipite, nambho mau yanga siyapita ata pang’ono."
Yesu wadamuyangha, "Yalembedwa, ‘Mundhu siwakhala wa moyo kwa bumundape, Nambho kwa kila malembo yoyela yakambidwa ni Mnungu.’"
Mwaeleche kwa uzene, mawu lanu nde zene.
Anyiimwe muyapenyechecha Malembo Yoyela kwa kuganizila kuti simpate umoyo wa muyaya kwa kuyapenyechecha, nambho malembo yaya yanichochela umboni ine!
Estudar e pregar
Os bereanos examinavam as Escrituras diariamente. Procura apresentar-te a Deus aprovado como obreiro que maneja bem a Palavra.
Ayahudi anyiyawa a ku Beloya amavechecha kupunda kupitilila wajha aku Sesalonike. Adakondwa kupunda yapo adauvela uthenga uwo adakambidwa ni Poolo, ni kila siku amatosoma Malembo ya Mnungu, kuona nagati icho wamakamba Poolo ni chazene.
Poolo wadalowa mnyumba yokomanilana Ayahudi, ngati umo lidali khalidwe lake. Wadakambilana ni wandhu nghani za Malembo Yoyela kwa Masiku yatatu yo Pumulila wadaakambila, uku ni wafotokozela malembo kwa kualangiza kuti Kilisito wamafunika kufa ni kuhyuka, niwakamba, "Uyu Kilisito nikukambilani nghani zake nde Yesu."
Ndiipo Filipo wadaithamangila ni kuiwandiikila ijha ngolo ni wadamuvela wamkulu yujha niwasoma chikalakala cha mlosi Isaya. Filipo wadamfunjha, "Bwanji, uvananavo ivo usoma?"
Wamkulu yujha wadayangha, "Nivananavo bwanji ngati palibe mundhu wonifotokozela ivo valembedwa?" Chimwecho wadamkambila Filipo wakwele mungolo mujha nikukhala pamojhi ni iye. Wamkulu mmeneyu wamasoma malembo yaya,
"Wadachogozedwa ngati mwana mbelele iyo ipita kuphedwa,
wadakhala chete ngati mwana mbelele yapo wadulidwa mabweya,
iye siwadachoche mvekelo ata pang’ono.
Ndiipo Filipo wadayamba kumkambila kupitila yajha malembo wamayasoma, pakumkambila Uthenga wa Yesu.
Ndiipo Yesu wadakambila, "Wandhu anyiimwe ni asabobwa kupunda. Niwolimba kukhulupilila icho chidalamebdwa ni alosi? Bwanji, siidafunike Kilisito uyo wasanghidwa ni Mnungu wavutike ni walowe mu ulemelelo wake?" Yesu wadafotokozela umo malembo yonjhe umo yakambila kuusu iye, kuyambila malembo ya Musa mbaka malembo ya alosi wina wonjhe.
Yesu wadajha pafupi pao ni kwaakambila, "Napachidwa ulamulilo wa kuchogoza kumwamba ni jhiko lapanjhi. Chipano pitani kwa wandhu maiko yonjhe, mkaachite kukhala oyaluzidwa, mkaabatize kwa jhina la Atate ni la Mwana ni la Mzimu Woyela, ni mwaayaluze kuyagwila yonjhe yayo nakulamulilani. Zenedi, ine nili pamojhi namwe muyaya mbaka mathelo ya jhiko la panjhi."
Pitani mkalalikile wandhu Uthenga uwu, ‘Ufumu wa kumwamba wawandikila.’
Revelação e fidelidade
A Palavra do Senhor veio aos profetas. A graça de Deus se manifestou na Escritura para a salvação de todos.
Viver pela Palavra
Não só de pão vive o homem. Nada acrescentes nem diminuas. A Palavra é alimento, guia e espada do cristão.
Uthenga wabwino ni umojhipe
Nizizwa kupunda ndande yandopitape ndhawi yochepa anyiimwe mwamsiya Mnungu uyo wadakutanani kwa ubwino wa Kilisito, anyiimwe mchata Uthenga wabwino wina uwo uoneka ngati Uthenga Wabwino. Zenedi asati Uthenga Wabwino. Uzene ni kuti alipo wandhu yawo akusakalichani, wandhu yao afuna kuyapundula mayaluzo ya Kilisito. Nambho ata ngati mmojhi wanu kapina mtumiki wa kumwamba wa Amnungu wakakulalikilani Uthenga wina uwo uoneneka ngati Uthenga Wabwino kusiyana ni ujha tidakulalikilani, walesedwe mundhu mmeneyo! Ngati mujha tidakukambilani, ni saino nikambanjho, ngati mundhu waliyonjhe wakakulalikilani Uthenga wina kusiyana ni ujha mdalikidwa, walesedwe mundhu mmeneyo!
Pakuti yonjhe yayo yadalembedwa mmalembo ya Mnungu, yadalembedwa ndande ya kutiyaluza ife, malembo yameneyo yatithangatila kulimba mtima mumavuto yathu ni kutitondeza, tikhoze kukhala ni chikhulupi.
Chipano sampembhe bwanji iye samkhulupilila? Nianyiiwo, samkhulupilile bwanji ngati sadavela nghani zake? Nisavele bwanji ngati palibe mundhu olalikila? Ni wandhu salalikile bwanji ngati sadapelekedwe? Ngati umo yalembedwa mmalembo ya Mnungu, "Chindhu chokwada kupunda kujha kwa wajha alalikila Uthenga Wabwino!" Nambho asati wonjhe adaulandila Uthenga Wabwino. Nde ndande Isaya wadakamba, "Mbuye ni yani uyo wadakhulupilila uthenga wathu?" Chimwecho, chikhulupi chichokana ni kuvela Uthenga Wabwino, ni uthenga umeneo uchokana ni mawu la Kilisito.
Mbhavu ya uthenga wa bwino
Ine siniona njhoni kuuzila uthenga wa Bwino, wene ni mbhavu ya Mnungu, iyo yaombola wandhu wonjhe amkhulupilila Yesu. Kuyambila Ayahudi ni anyiawo osati ayahudi. Pakuti uthenga wa bwino walangiza umo Mnungu wafunila tikhale kuti tivomelezeke pachogolo pake, chindhu ichi chichitika kwa kumkhulupilila Yesu Kilisito, palibe china kupitilila chimecho, ngati umo yalembedwa mmalembo, "Mundhu wovomelezeka kwa Mnungu siwakhale kwa kumkhulupilila Mnungu."
Sitidalandile Mzimu wa jhiko nambho ife talandila Mzimu ujha wachokela kwa Mnungu, chimwecho sitijhiwe vonjhe ivo Mnungu watipacha ife.
Chimwecho sitikamba kwa mau ayaluza ali ni hekima, nambho mau wa yaluza Mzimu wa Mnungu, tikambilila vindhu va Uzimu kwa onjhe ali ni Mzimu wa Mnungu. Uyo walibe Mzimu wa Mnungu siwakhoza kulandila mbhaso ikujha kuchokela kwa Mzimu wa Mnungu. Mundhu mmeneyo siwakhoza kuva yameneyo, waona kuti vindhu vimenevo vilibe mate, ndande yake yavunukulidwa muchizimu.
Mnungu ni wa hekima, wandhu sakhoza kumjhiwa Mnungu kwa kukhulupilila hekima yao achinawene. Chimwecho Mnungu wadautumila uthenga wa Yesu Kilisito uwo uoneka kuti ulibe mate, nambho anyiwajha aukhulupilila uthenga umenewo aomboledwa.
Ayahudi afuna vizindikilo dala akhulupilile, ni Agiliki afuna hekima. Nambho ife timlalikila Kilisito uyo wadapachikidwa, kwa Ayahudi chindhu ichi ni choipicha, ni kwa Agiliki chopande mate. Nambho kwa anyiyawo atanidwa ni Mnungu Ayahudi kwa Agiliki, Kilisito uyu wadapachikidwa ni mbhavu ya Mnungu ni hekima ya Mnungu.
Kilisito siwadanitume kubatiza. Wanituma kulalikila Uthenga Wabwino, nilalikile popande kukhulupilila mawu ya hekima za wandhu, dala mbhavu ya nyifa ya Kilisito pamtanda siidaoneka yopandemate.