Pular para o conteúdo
Publicidade

Pensamentos

Por Bíblia Online

A Bíblia ensina que somos fruto dos nossos pensamentos. Por isso, Deus nos chama a renovar a mente, pensar em coisas nobres e guardar o coração com toda diligência.

Pensar no que é bom

Paulo nos exorta a pensar no que é verdadeiro, honesto, justo, puro, amável e de boa fama. A mente renovada é o caminho da transformação.

Potela mpenye vindhu vazene, ni yamate, yavomeleka, yaelecheka, yakhadwa ni yaulemu.

Simudaganizila ngati wandhu ajhiko lino umo aganizila, nambho Mnungu siwakung’anamuleni maganizo yanu kwa kuganizila bwino. Pamenepo ndipo simkhoze kujhiwa icho wafuna Mnungu ni kujhiwa chindhu chili cha bwino, ilo limkwadilicha ni kuchita ngati umo ifunikila.

Iye uyo wakhoza kuchita vindhu vodabwicha kupunda kupitilila vijha tivipembha ni kuvighanizila. Kuchokana ni mbhavu zake izo zichita njhito mkati mwathu. Watamandidwe, ulemelelo wake ukhale kwa gulu la wandhu wonjhe akhulupilila Kilisito ni kwa Kilisito Yesu ndhawi zonjhe, Muyaya ni muyaya! Ikhale chimwecho.

Guardar a mente

A Palavra de Deus discerne os pensamentos e intenções do coração. Guardar a mente é proteger a alma das armadilhas do pecado.

Os caminhos de Deus são mais altos

Os pensamentos de Deus são infinitamente superiores aos nossos. Devemos entregar nossos pensamentos a Ele e confiar em sua sabedoria.

Pensamento e conduta

Do coração procedem os males. A Bíblia nos adverte a não se preocupar excessivamente e a ter pensamentos sóbrios e disciplinados.

Wadaendekela kukamba, "Icho chichoka mkati mwa mundhu nde chimchita mundhu siwadavomelezeka kumlambila Mnungu. Pakuti kuchokela mmitima ya wandhu, yachoka maganizo yoipa ni chigololo ni unghungu ni kupha, uhule ni khumbilo lo funa chuma chambili ni voipa ni unami ni kukafula ni khumbilo lofuna chigololo ni mbwinya ni usabwabwa. Voipa vimenevo vichoka mkati mwa wandhu, navo vimchita mundhu siwadavomelezeka kumlambila Mnungu."

"Ndendande nikukambilani msadajhichaucha pa umoyo wanu kuti simudye chiyani kapina simumwe chiyani kuti mkhale amoyo kapina mathupi yanu simuvale chiyani. Bwanji umoyo osati wa phindu kupitilila chakudya? Bwanji, thupi lilibe phindu kupitilila vivalo?

"Yapo upembhela usadakamba mawu yambili ngati wandhu yawo samjhiwa Mnungu. Anyiiwo aganiza kuti siwaavele ndande ya kuchuluka kwa mawu yawo.

Yesu wanyindila wandhu yawo ajhichita kuti amtumikila Mnungu

Ndhawi imeneyo, wandhu wochuluka yapo adasonghana mbaka amapondana, Yesu wadayamba kukamba ni oyaluzidwa wake, niwakamba, "Mkhale maso, musadachita ngati Afalisayo, yawo ajhichita kuti amchata Mnungu. Palibe icho chabisidwa sichiikidwa padanga, ni palibe icho chavinikilidwa sichivukulidwe. Chimwecho, icho mwachikamba kumdima, sichivekele padanga, ni icho mwachinong’ona mmakhutu kuvyumba vanu, sichiuzilidwe pandhandala."

Uyo wafunika kuopedwa

"Nikukambilani anyiimwe achabwenji langa, msadawaopa anyiyawo akupha thupi, anyiyawo pambuyo pa yameneyo saakhoza kuchita chilichonjhe. Nambho, sinikulangizeni uyo mufunika kumuopa, muopeni yujha pambuyo pakupha thupi wakhoza kukuponyani kumoto wosathima muyaya. Zenedi nikukambilani, muopeni iye. Bwanji, njhwala zisano sizigulichidwa kwa mtengo waung’ono kupunda? Nambho, pamaso pa Mnungu siiwalika ata njhwala imojhi. Zenedi, ata machichi ya mmitu yanu, yawelengedwa. Chipano, msadaopa, anyiimwe nde muli ni phindu kupunda kupitilila njhwala!"

Kumuuzila ni kumkana Yesu

"Nikukambilani uzene, kila uyo wauzila pamaso pa wandhu kuti wali pamojhi ni ine, Mwana wa Mundhu naye siwamuuzile kuti mundhu mmeneyo wali pamojhi niiye pamaso pa atumiki akumwamba a Mnungu. Nambho, mundhu waliyonjhe uyo siwanikane pamaso pa wandhu, Mwana wa Mundhu naye siwamkane pamaso pa atumiki akumwamba a Mnungu."

Waliyonjhe uyo wakamkambila mawu yoipa Mwana wa Mundhu, siwalekeleledwe, nambho waliyonjhe uyo siwamtukwane Mzimu Woyela, siwalekeleledwa.

"Yapo sakupelekeni mnyumba ya mapembhelo ya Ayahudi, kapina pamaso pa wakuluakulu ni alamuli kuti mulamulidwe, msadajhifunjha umo simujhitetezele. Ndande yake, Mzimu Woyela siwakuyaluzeni icho simufunike kukamba ndhawi imeneyo."

Chifani cha mundhu wopata sabobwa

Mundhu mmojhi pakati pagulu la wandhu lijha, wadamkambila Yesu, "Oyaluza, mkambileni mkulu wanga kuti tigawane chuma icho adatilekela atate wathu." Nambho, Yesu wadayamuyangha, "Bwenji wanga, yani uyo wanisanghula ine kuimilila ni kugawana kwanu chuma cha atate wanu?"

Ndiipo Yesu wadaakambila wandhu wajha, "Mujhipenyelele ni chipili vindhu vonjhe, pakuti umoyo wa mundhu siupatikana ndande ya kuchuluka kwa chuma icho walinacho mundhu." Ndiipo Yesu wadapacha chifani, "Kudali ni wopata mmojhi uyo wadali ni munda uwo udabala vipacho vochuluka. Mundhu wopata mmeneyo wadayamba kuganizila mumtima mwake, Nichite chiyani? Pakuti nilibe malo yosungila chakudya changa icho nachikolola. Sinigomole nghokwe zanga ni kumanganjho zazikulu kupitilila ni mmenemo, nde umo siniikemo vokolola vanga vonjhe ni chuma changa.Pamenepo siniukambile mzimu wanga, Chipano uli ni chuma cha mbili, ivo udavisunga kwa vyaka vambili. Pumulila, udye, umwe ni kukondwela.Nambho Mnungu wadamkambila, Wopusa iwe! Umoyo wako siutengedwe usiku uno. Ni vindhu vonjhe ivo wajhiunjikila sivikhale vayani?"

Yesu wadakamba, "Umu nde umo ili kwa yawo ajhiunjikila chuma cha mbili mwene wake, nambho alibe chindhu icho chili chokhadwa pamaso pa Mnungu."

Kumkhulupilila Mnungu

Ndiipo Yesu wadakambila oyaluzidwa wake, "Chimwecho, msadajhichaucha kuusu umoyo wanu kuti simdye chiyani, kapina ndande ya matupi yanu kuti simvale chiyani. Chifuko, umoyo ni wofunika kupunda kupitilila chakdya, ni thupi nilofunika kupunda kupitilila vovala. Penyani khungubwe, izo sizivyala kapina kukolola, zilibe nghokwe kapina malo yaliyonjhe yosungamo chakudya, nambho Mnungu wazidyecha. Anyiimwe ni abwino kupunda kupitilila mbalami! Yani pakati panu wakhoza kuonjezela umoyo wake ingakhale kwa saa limojhipe? Pakuti, mlepela kuchita chindhu chaching’ono ngati ichi, ndande yanji mujhivuticha kuchita ivo vili vavikulu vimenevo? Penyani maduwa umo yakulila. Siyachita njhito kapina kujhikhwadilicha, nambho nikukambilani ata Mfumu Solomoni uyo wadavala vivalo vabwino kupunda, siwadajhikadwiliche ngati limojhi la maduwa yaya. Chipano, ngati Mnungu wayaveka nchimwecho maduwa ya kuthengo, yayo yamela lelo ni mawa yakugwa ni kutaidwa pamoto, bwanji, sisakuvekeni anyiimwe bwino kupunda, wandhu achikulupililo chochepa!

"Basi, msadajhisaucha mmitima yanu, kuti mukudya chiyani kapina mukumwa chiyani. Pakuti yameneyo yachauchilidwa kupunda ni wandhu wonjhe yawo samjiwa Mnungu. Nambho, Atate wanu a kumwamba ayajhiwa kuti muyafuna. Nambho, ufunefuneni uti ufumu wa Mnungu, ni vindhu ivi navo simupachidwe."

Kujhiikila chuma kumwamba

"Msadaopa, anyiimwe muli gulu laling’ono, pakuti Atate wanu akonda kukupachani anyiimwe Ufumu wao. Gulichani vyuma vanu ni mwaninghe ndalama wandhu wosauka ndalama zimenezo. Mujhikonjele matumba ya ndalama yosatha ni ikilani chuma kumwamba icho sichichepa, kumalo uko anghungu sakhoza kuba ni vidudu kuwananga. Ndande yake, yapo waikila chuma chako ndeyapo umoyo wako siukhalepo."

Khalani maso

"Mkhale tayali kupota njhito ni musiye nyali zanu ni ziwala, Mkhale ngati atumiki yawo amlindilila bwana wawo uyo wabwela kuchokela ku ukwati, kuti yapo siwachakulize chicheko, amchakulile chisanga. Mbowa wajha siakondwele mbuye wawo yapo siwapheze atomlindilila. Zenedi nikukambilani, bwana mmeneyo siwavale vivalo va mbowa ni kwakambila kuti mkhale niine sinikutumikileni. Mbowa wajha siakondwele mbuye wawo wakaapheza ali tayali kumlandila ata ngati siwajhe usiku kupunda kapina mmalengakucha. Nambho nifuna mujhiwe chindhu ichi, ngati mwene khomo wadakajhiwa ndhawi uyo wakuba siwajhe, wadakakhala maso, siwadakasiya nyumba yake igomoledwe. Chimwecho, namwenjho mukhale wokonjeka nyengo zonjhe, pakuti Mwana wa Mundhu siwajhe ndhawi iyo anyiimwe simuiijhiwa."

Mbowa wokhulupilika

Ndiipo Petilo wadamfunjha Yesu, "Ambuye, chifani ichi chitihusu ife tekha, kapina kwa wandhu wonjhe?" Ambuye adayangha, "Mbowa yuti uyo wali wokhulupilika ni wa njelu, uyo waikidwa ni bwana wake kwaimilila kila kandhu kake, kuti wagawile chakudya pa ndhawi iyo ifunika? Siwakhale wokondwa mbowa uyo bwana wake yapo sabwele sampheze niwachita chimwecho. Nikukambilani uzene, siwamuike waimilile vindhu vake vonjhe. Nambho, ngati mbowa mmeneyo siwaganizile mumtima mwake kuti mbuye wake wachedwa kubwela, ni kuyamba kwamenya mbowa wina yawo waimilila, wachimuna ni wachikazi, ni uku niwadya, ni kumwa ni kulojhela, bwana wake siwabwele siku ilo siwalijhiwa iye. Siwampache chilango chachikulu kupunda mbowa mmeneyo ni kumuika pamojhi ni wosakhulupilika."

"Mbowa uyo wajhiwa ivo afuna bwana wake, nambho siwachita yayo afuna bwana wake kuti wayachite, mbowa mmeneyo siwalangidwe chilango chachikulu kupunda. Ni mundhu waliyonjhe uyo siwajhiwa icho chifunika kuchita, niwakachita vindhu ivo wafunika kulangidwa, siwapachidwe chilango chachiang’ono. Pakuti, mundhu uyo wapachidwa vambili, siwadaidwe vambili, ni mundhu uyo wapachidwa ulamulilo waukulu ni mundhu mwina, siwafunjhidwe kopitilila."

Yesu wapeleka kupatukana

"Nafika kujha kukweleza moto pajhiko, ni ine nikhumbila kuti udakakhala wathokwelela! Nambho nili ni mavuto yayakulu yayo nifunika kuti nivutike, nambho nichauchika kupunda mbaka yapo siyakwanile! Msadaganiza kuti najha kupeleka mtendele pajhiko la panjhi? Notho! Najha kupeleka kupatukana. Ni kuyambila chipano, wandhu asano ambadwa umojhi siapatukane, wandhu atatu siabulane ni wandhu awili, ni awili sabulane ni wandhu atatu. Atate siapatukane ni mwana wao, ni wana wao sapatukane ni atate wao, amayi sapatukane ni mwana wao wamkazi ni mwana wao wamkazi sapatukane ni amayi wake, ni mpongozi wamkazi sapatukane ni apongozi wake wakazi."

Kujhiwa nyengo

Yesu wadalikambilanjho gulu lijha lawandhu, "Yapo muona mitambo niyachokela kumpoto, kwamkamojhi mkamba kuti vula siinye, ni ikunyadi. Ni yapo muona mbhepo kuchokela kunyanja, mkamba kuti sikukhale kofunda, ni ikhaladi chimwecho. Anyiimwe agunghuli! Muzijhiwa nyengo kwa kupenya mlengalenga, chifuko chiyani simjhiwa mate ya vindhu vichokela saino?"

Uvane ni adani wako

"Ndande yanji mlepela kulamula mwachinawene icho chili chabwino? Yapo upita ni mdani wako kunyumba ya milandu, ujhitaidi kuvana naye muli mnjila. Ngati siuchita chimwecho siwakupeleke kwa mbhavu kwa mlamuli, ni mlamuli siwakupeleke kwa asikali ni asikali siakuike mndende. Zenedi nikukambila, siuchoka mndende mbaka yapo siulipile ndalama yothela."

Kuchokana ni ubwino uwo wanipacha Mnungu, nikukambilani anyiimwe mwaonjhe, simdajhiona kuti anyiimwe ni abwino kusiyana ni umo mmafunika kukhala. Mjhipime mwachinawene umo muli kwa chipimo cha chikhulupi icho Mnungu wamgawila kila mmojhi,

Kupatukana kwa Wandhu amkhulupilila Yesu

Kwa ulamulilo wa Ambuye wathu Yesu Kilisito nikupembhani kupunda, achabale wanga, mvanichane kwa kila chindhu icho mukamba, sikudakhala ni kupatukana pakati panu, mukhale ni maganizo yamojhi ni dala imojhi.

Palibe mundhu uyo wajhiwa maganizo ya mundhu mwina. Chimchijha mzimu wokha ulimkati nde ujhiwa maganizo ya mundhu mmeneyo, chimwecho ndeumo ili ata kwa Mnungu, Mzimu wokha wa Mnungu nde ujhiwa maganizo ya Mnungu.

Msadajhinamiza, ngati mwina wanu wakajhiganiza waima pa jhiko, wafunika wakhale owowela kuti wapate kukhala ni hekima.

Seja o primeiro