Pular para o conteúdo
Publicidade

Santa ceia

Por Bíblia Online

A Santa Ceia é uma das ordenanças mais sagradas da igreja cristã. Instituída por Jesus na última noite antes da crucificação, ela celebra seu sacrifício e proclama sua morte até que Ele volte.

A instituição por Jesus

Na noite em que foi traído, Jesus tomou o pão e o cálice, deu graças e os compartilhou com os discípulos, dizendo: 'Fazei isto em memória de mim.'

Chakudya cha Ambuye

Yapo amadya Yesu wadatenga bumunda, wadayamika, wadaubandhula, ni kwapacha oyaluzidwa wake nikukamba, "Tengani mudye, ili nithupi langa."

Ndiipo wadatenga chikho, wadayamika Mnungu, ni kwaapacha oyaluzidwa wake niwakamba, "Mwaonjhe mchimwele chikho ichi, uwu nde mwazi wanga uwo uchimikiza chipangano, umwazika ndande ya ambili dala machimo yao yalekeleledwe.

Chakudya cha Ambuye

Yapo amadya, Yesu wadatenga bumunda, wadamuyamika Munungu, wadaubandhula ni kwapacha oyaluzidwa wake uku ni wakamba, "Tengani, mudye ili ni thupi langa." Ndiipo wadatenga chikho cha divai, wadamuyamika Mnungu, wadaapacha, wonjhe adachimwela. Wadaakambila, "Uwu ni mwazi wanga uwo uchimikiza chipangano cha Mnungu, mwazi uwo umwazika ndande ya wandhu ambili. Zenedi ni kukambilani, sinimwa divai mbaka siku lijha yapo siniimwenjho divai yachipano ku Ufumu wa Mnungu."

Ndiipo, wadatenga bumunda, wadayamika, ni kuubandhula, wadapacha atumwi ni kukamba, "Ili ni thupi langa ilo lichochedwa ndande ya anyiimwe. Mjichite chimwechi ponikumbukila ine." Chimwecho, yapo adamaliza kudya, wadachita chimchijha wadatenga chikho chija ni kukamba, "Divai iyi ili mchikho ni chipangano cha chipano icho chichitidwa kwa mwazi wanga, uwo umwazika ndande yanu."

O significado espiritual

A Ceia é participação no corpo e no sangue de Cristo. Jesus ensinou que quem come de sua carne e bebe de seu sangue tem a vida eterna.

Ine nde chakudya chili cha moyo icho chachika kuchoka kumwamba. Mundhu waliyonjhe uyo siwadye chakudya ichi siwakhale moyo muyaya. Ni chakudya icho sinimpache, nde thupi langa ilo nichocha ndande ya wandhu ajhiko la panjhi."

Ndiipo Yesu wadaakambila, "Zene nikukambilani, mkasiya kudyaa thupi la mwana wa Mundhu ni kumwa mwazi wake, simukhala ni umoyo mkati mwanu. Kila mmojhi uyo siwadye thupi langa ni kumwa mwazi wanga wali ni umoyo wa muyaya, nane sinimuhyuche siku lo thela. Ndande thupi langa nde chakudya cha uzene, ni mwazi wanga nde chakumwa cha uzene. Uyo wakudya thupi langa ni kumwa mwazi wanga, siwakhale mkati mwanga, nane sinikhale mkati mwake. Ngati umo Atate yawo ali amoyo adanitumila, nane nili wamoyo kupitila iwo, chimwecho uyo waniidya ine siwakhale moyo kupitila ine. Chino nde chakudya icho chachika kuchoka kumwamba, osati ngati mana iyo adadya azee wanu, ndiipo adamwalila. Uyo wakudya bumunda lino siwakhale moyo muyaya."

wadamuyamika Mnungu, wadaubandhula, wadakamba, "Ili nithupi langa, ilo lachochedwa ndande yanu. Chitani chimwechi kwa kunikumbukila." Chimwechijha, pambuyo pakudya wadatenga chiko niwakamba, "Chikho ichi ni chipangano cha chipano cha Mnungu, chichimikizidwa kwa mwazi wanga. Chitani chimwechi kila yapo mkumwa, kwa kunikumbukila."

Pakuti kila yapo simujhidya bumunda ili ni kumwa mchikho ichi, muuzila wina Ambuye adafa ndande yanu mbaka yapo siwajhe. Chimwecho, kila uyo wakudya bumunda la Ambuye, ni kumwa mchikho ichi ngati umo siifunikila, siwakhale wachita machimo kwa thupi ni mwazi wa Ambuye. Ifunika, mundhu wajhipenyecheche mwene, ukali osadye bumunda ni kumwa mchikho.

Pakuti kila yapo simujhidya bumunda ili ni kumwa mchikho ichi, muuzila wina Ambuye adafa ndande yanu mbaka yapo siwajhe.

A prática da Igreja

Desde os primeiros cristãos, a Ceia do Senhor é parte fundamental da vida comunitária da Igreja, celebrada com reverência e exame de consciência.

Wonjhe adali kuvechela mayaluzo ya atumwi kila siku, amakomana pamojhi niadya chakudya cha Ambuye ni kupembhela.

Poolo wamuhyukicha Elitiko

Siku limojhinla jhuma, tidakomana pamojhi kuti tidye chakudya. Poolo wamauzila wandhu ni kuyendekela kukamba nawo mbaka usiku pakati, pakuti wadafuna kuchoka siku lochatila.

Yapo wadakhala kudya chakudya pamojhi ni anyiiwo, iye wadatenga bumunda ni kwayamika Amnungu, wadaubandhula nikwaapacha.

Chimwecho, kila uyo wakudya bumunda la Ambuye, ni kumwa mchikho ichi ngati umo siifunikila, siwakhale wachita machimo kwa thupi ni mwazi wa Ambuye. Ifunika, mundhu wajhipenyecheche mwene, ukali osadye bumunda ni kumwa mchikho. Pakuti mundhu uyo wakudya ni kumwa, popande kujhiwa mate ya thupi la Ambuye, kwa kuchita chimwecho Mnungu siwakulange.

Seja o primeiro